Tsamba 2
Mabanja a Kholo Limodzi—Kodi Angakhale Achipambano Motani? 3-9
Lerolino mabanja ambiri ali ndi kholo limodzi lokha lolera ana. Kodi angathandizidwe motani?
Kodi Miyezo ya Mulungu ndi Yosafikirika? 14
Kodi Mulungu waika miyezo yake kukhala yapamwamba kwambiri kwakuti anthu opanda ungwiro sangaifikire?