Tsamba 2
Nchifukwa Ninji Moyo Uli Waufupi Motere?—Kodi Udzasintha Konse? 3-11
Nchifukwa ninji timakalamba? Nchifukwa ninji timafa pambuyo pa zaka ngati 70 kapena 80, ngakhale kuti mathupi athu mwachionekere anapangidwa kuti akhale kosatha? Kodi tikhozadi kukhala ndi moyo kosatha?
Chipolopolo Chinasintha Moyo Wanga 12
Dziŵani za mmene chipolopolo chosokera chinasinthira kwambiri moyo wa msungwana wina. Mudzalimbikitsidwa chifukwa cha kuyesayesa kwake kufikira zonulirapo zake.