Tsamba 2
Kodi Mulungu Amalola Chipembedzo Kuloŵa m’Nkhondo? 3-11
M’mbiri yonse, anthu aphana m’dzina la Mulungu. Kodi tingati kuphana kumeneko kuli bwino? Kodi Mulungu amaganizapo bwanji?
Kuzenga Mlandu “Wopandukira Tchalitchi” ndi Kumnyonga 12
Bwalo la Inquisition la Akatolika linapha anthu zikwizikwi. Nchifukwa ninji tchalitchi chinalola chiwawa chimenechi?
Tasmania—Chisumbu Chaching’ono, Nkhani Yake Yapadera 18
Kodi nchifukwa ninji Tasmania anakhala dziko la ndende la Britain? Kodi Abritishi anachita nawo motani Aaborijini? Kodi moyo ngwotani m’Tasmania wamakono?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Kuchikuto: Alexandra Boulat/Sipa Press
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Bibliothèque Nationale, Paris
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
The Complete Encyclopedia of Illustration/J. G. Heck