Zisonyezero za Voliyumu 78 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Bwenzi Langa Linasamukiranji? 1/8
Kodi Mulungu adzakhalabe Bwenzi Langa? 6/8
Kuchita Mfunzi—Kumavulaza Motani? 4/8
Kudwala, 7/8
Kuimbidwa Mlandu? 8/8, 9/8
Kukhala Bwenzi la Mulungu, 3/8
Kukondera? 12/8
Kupeza Ndalama? 10/8
Nchifukwa Ninji Amamuikako Nzeru? 11/8
Ndiulule Tchimo Langa? 2/8
CHIPEMBEDZO
Chipembedzo Kuloŵa M’nkhondo, 5/8
Kuzenga Mlandu “Wopandukira Tchalitchi” ndi Kumnyonga, 5/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Chigumula—Chenicheni Kapena Nthano? 2/8
Dziko Lapansi Lidzathera m’Moto? 1/8
Kodi Akristu Ayenera Kuda Ochita Mathanyula? 12/8
Kodi Akristu Ayenera Kukhala Otsutsa Nkhondo? 5/8
Kodi Ana Ayenera Kudzisankhira Chipembedzo? 3/8
Kuba kwa Wosauka Nkololeka? 11/8
Kudzimana Ndiyo Njira Yopezera Nzeru? 10/8
‘Kusakhala a Dziko Lapansi,’ 9/8
Nkotheka Kupulumutsa Ukwati? 4/8
Nkulakwa Kudya Nyama? 8/8
Nkulamuliriranji Mkwiyo? 6/8
Sayansi ndi Baibulo Zimagwirizana? 7/8
MAIKO NDI ANTHU
Chigwa cha Great Rift Valley, 8/8
Kusema Ziboliboli—Luso Lakale mu Afirika, 10/8
Ng’oma za mu Afirika, 8/8
Nkhalango Yamvula ya Amazon, 4/8
Nkhondo za Chipembedzo ku France, 5/8
Singapore—Ngale Yowonongeka ya Asia, 6/8
Tasmania, 5/8
MAUNANSI A ANTHU
Ana Osakhoza Kuphunzira, 3/8
Choonadi Ponena za Bodza, 3/8
Kodi Kholo Ndani? Nanga Mwana Ndani? 10/8
Kulolera Kopambanitsa? 2/8
Kusamala Wina, 2/8
Mabwenzi Odalirana (galu wotsogoza wakhungu), 5/8
Thandizani Ana Anu Kukula Bwino, 8/8
Woyenera Kusunga Ana, 12/8
MBONI ZA YEHOVA
Mabwenzi Odalirana (A. Evaldsson), 5/8
Russia, 9/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Kutengapo Phunziro pa Mphika wa Mafuta (K. Hahn), 11/8
Tsoka la Maggy Ndi Dalitso Langa (L. Wilkins), 1/8
Wokondwa Kukhala ndi Moyo! (G. Klauss), 5/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Khalidwe Loipa, 8/8
Kusamala Wina, 2/8
Kuteteza Thanzi la Ana, 10/8
Likodzo, 3/8
Mapazi Akamawawa, 10/8
Miliri, 12/8
Njira Zotetezera Thanzi, 12/8
Nzeru ya Kupeŵa Kugonana ndi Kukwatirana ndi Munthu Mmodzi Yekha, 6/8
Wokondwa Kukhala ndi Moyo, 5/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Kodi Galu Wanu Sangavulaze Ana? 7/8
Kupulumutsa Nyama, 7/8
Minda ya Maluŵa, 4/8
Tulo ta Nyama, 12/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Akuba, 10/8
Chakudya cha Onse—Kodi ndi Loto Chabe? 8/8
Chimene Nkhondo Zimachita kwa Ana, 11/8
Kugulitsa Ana mu Uhule, 4/8
Kusintha Maganizo pa za Kugonana, 6/8
Miliri, 12/8
Nchifukwa Ninji Pali Chidani Chochuluka? 9/8
Phokoso, 11/8
Umbombo—Mmene Umatikhudzira, 1/8
Upandu Wolinganiza, 3/8
Vuto la Madzi 9/8
ZOSIYANASIYANA
Chimapatsa Anthu Chimwemwe Nchiyani? 11/8
M’Khichini Mungakhale Mosangalatsa, 1/8
Munda wa Dziko Lonse, 4/8
Paradaiso Wopanda Mavuto, 10/8
Ŵerengerani Mtengo wa Kusamuka! 5/8