Tsamba 2
Magulu Aupandu a Mumsewu—Mliri Wadziko Lonse Womwe Ukufala 3-11 Kodi Nchifukwa Ninji Achinyamata Ambiri Amaloŵa M’magulu Aupandu? Kodi Nchifukwa Ninji Kuli Kovuta Kwambiri Kutuluka M’gulu Laupandu? Kodi Ana Anu Mungaŵateteze Bwanji Ku Magulu Ameneŵa?
Ulendo Wanga Wautali Kuchokera pa Moyo Wangozi m’Cambodia 12
Wathana Meas anali mmonke wachibuda ndipo kenako anadzakhala ofesala wa gulu lankhondo ku Cambodia. Nkhani yake ili ngati ulendo wautali wokafunafuna chipulumutso.
Kodi Chaka cha 2,000 Chidzawakhudza Bwanji Anthu? 30
Kodi Baibulo limatchula chaka chimenecho? Kodi Akristu ayenera kumadera nkhaŵa za detilo?