Tsamba 2
Kumwa Mankhwala Panokha—Kodi Kungakuthandizeni Kapena Kungakuvulazeni? 3-9
Kumwa mankhwala mosauzidwa ndi dokotala tingati ndiyo njira yokha yothandizikira yomwe ilipo m’madera ambiri amene ali kwa okhaokha padziko lapansi. M’maiko ena, pali njira zambiri zothandizikira. Koma kodi nchiyani chofunika kusamala posankha mankhwala amene mugwiritsire ntchito?
Kodi Nkulakwa Kuseŵera Kokopana Pakati pa Mwamuna ndi Mkazi? 16
Kodi pali kusiyana kwanji pakati pa kukhala chabe waubwenzi ndi kuseŵera mokopana? Nchifukwa chiyani kuseŵera kumeneku kuli koopsa ndiponso nkudzikonda?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
© The Curtis Publishing Company