Tsamba 2
Moyo Wotetezereka Kosatha—Mungaupeze Motani? 3-10
Anthu ambiri akuona kuti miyoyo yawo ndiponso chikhalidwe chawo zili pangozi ndipo nzosadalirika. Kodi tingayembekezere kuti tidzakhala moyo wotetezereka? Inde, moyo wotetezereka wayandikira!
Kodi Ndingatani Kuti Ndizimvetsera Mwachidwi? 22
Ŵerengani mmene mungachitire kuti muyambe kumamvetsera mwachidwi mwakungosintha pang’ono khalidwe lanu.
Ubwino Wakukhala Panokha 30
Kodi lingaliro la Baibulo ndi lotani ponena za mapindu ndi kuipa kwa kumakhalako panokha?