Tsamba 2
Kodi Anthu Onse Adzakhala ndi Ufulu Wachibadwidwe? 3-14
Kwa anthu mamiliyoni ambiri padziko lonse lapansi, kulandidwa ufulu wawo, monga mwa tsankho, kuzunza ana, ndi ukapolo, zimawachitikira masiku onse. Kodi ufulu wa anthu onse udzathekadi padziko lonse lapansi?
“Mutha Kusiya—Ifenso Tinasiya!” 15
Kodi nchiyani chinawasonkhezera anthuwa kusiya kusuta fodya?
Kodi Miyala Yamlengalenga Idzagunda ndi Kuwononga Dziko? 30
Kodi Baibulo limati bwanji?