Tsamba 2
Kodi Moyo Wanu Ukukuvulazani? 3-11
Thanzi labwino lathupi, ndi lauzimu komanso maganizo abwino angakhale maziko a moyo wachimwemwe ndi wautali. Kodi moyo wanu ukukukhudzani Motani?
Okonda Kuothera Dzuŵa—Tetezani Khungu Lanu! 16
Khungu n’chiŵalo chotiteteza chofunika kwambiri, koma nachonso chimafuna kutetezedwa. Taŵerengani kuti mudziŵe chifukwa chake, ndipo phunzirani mmene mungakhalire wosamala ngati mwakhala padzuŵa.
Mulungu Wakhala Mthandizi Wathu 20
Ŵerengani nkhani yochititsa chidwi yonena za anthu zikwizikwi amene anali m’misasa ku Mozambique, ndipo onani mmene anakhalira okhulupirika kwa Mulungu.