Tsamba 2
Kodi Mankhwala Osokoneza Bongo Akulanda Dziko? 3-14
Malonda a mankhwala osokoneza bongo ozembera boma komanso kugwiritsa ntchito mankhwalawo kumatikhudza tonse, mwachindunji kapena m’njira zina. Kodi pangachitike chiyani kuti pasakhalenso anthu ogulitsa ndi ofuna mankhwalawa?
Kodi Chimachititsa Ufiti N’chiyani? 30
Mfiti ndi misonkhano ya afiti, m’chaka cha 1999? Kodi n’chifukwa chiyani anthu ena amakopeka ndi ufiti?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Godo-Foto