Tsamba 2
Zaka za Zana la 20—Zaka za Kusintha Kwakukulu 3-12
Kusintha kwakukulu kwachitika m’zaka za m’zana la 20. Komabe, chimodzi mwa zinthu zofunika kwambiri zimene zasintha anthu ambiri achinyalanyaza. Kodi ndi chiyani?
Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale Wochezeka? 13
Kodi mumachita manyazi? Talingalirani mfundo zina zimene zingakuthandizeni kuthetsa manyazi.