Zisonyezero za Voliyumu 80 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Chibwenzi ndi Munthu Amene Akukhala Kutali, 2/8
Kukhala Wochezeka? 11/8, 12/8
Kupirira Kusoŵa Chilungamo? 10/8
Kutonzedwa, 7/8
Maseŵero Odziyerekeza Kukhala Munthu Wotchuka, 9/8
Miseche, 3/8
N’chifukwa Chiyani Amayi Anga Akudwala Chomwechi? 8/8
N’chifukwa Chiyani Ndimaopa Kunenepa? 5/8
N’chifukwa Chiyani Sindikutha Kupeza Zinthu Zimene Ndimafuna? 4/8
Ndingakhale Motani Wopanda Makolo? 1/8
Vuto Loopa Kunenepa, 6/8
CHIPEMBEDZO
Kodi Mukufuna Kukondweretsa Mulungu? 1/8
Kodi Mulungu Alikodi? 2/8
Kukambirana za Chipembedzo, 3/8
N’chikonzero cha Mulungu? 8/8
Ufulu Wachipembedzo Ukuponderezedwa, 1/8
Wosakhulupirira Mulungu Apeza Mayankho, 12/8
CHUMA NDI NTCHITO
Malonda Apadziko Lonse, 9/8
Yuro—Ndalama Yatsopano, 5/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Kodi Akufa Ayenera Kulemekezedwa? 2/8
Kodi Chimachititsa Ufiti N’chiyani? 11/8
Kodi Mzimu Woyera wa Mulungu N’chiyani? 1/8
Kodi Nzika Yabwino Imakhala Yotani? 9/8
Kugwirizana pa Zachipembedzo m’Banja, 8/8
Kunyada N’kulakwa? 7/8
Kusankha Wokwatirana Naye, 10/8
Mafumu Atatu Anakaona Yesu ku Betelehemu? 12/8
Misa (Yachikatolika), 5/8
Ndinu Wofunika Kwambiri kwa Mulungu! 6/8
N’kulakwa Kutchula Dzina la Mulungu? 3/8
MAUNANSI A ANTHU
Agogo, 4/8
Asonyezeni Kuti Mumawakonda (achikulire), 4/8
Kalata kwa Makolo Awo (Spain), 3/8
Kusankha Wokwatirana Naye, 10/8
Pamene Mwamuna Kapena Mkazi Akhala Wosakhulupirika, 5/8
MAYIKO NDI ANTHU
India ndi China Akuwonongedwa ndi Fodya, 11/8
Malo Otchuka Achikale Otchedwa Vinland, 7/8
Ndalama ya mu Afirika (peni ya Kissi), 4/8
Njira ya ku Afirika Yopangira Chiponde, 9/8
Phiri la Sinai—Mwala Wokongoletsa Chipululu, 5/8
MBONI ZA YEHOVA
Akazi Anachita Mbali Yaikulu (Zimbabwe), 7/8
Analimbikitsidwa ndi Chikhulupiriro cha Iye, 11/8
“Chikhumbo Changa Chachikulu,” 10/8
Galamukani! Ithandiza Kujambula Chikwangwani Choletsa Kusuta Fodya, 7/8
‘Imapindulitsa Bwanji Anthu?’ 6/8
Kalata kwa Makolo Awo (Spain), 3/8
Mbewu Zimene Zinabala Zipatso Patapita Zaka Zambiri, 7/8
Msonkhano wa za Opaleshoni Yopanda Magazi (Moscow), 5/8
Mulungu Wakhala Mthandizi Wathu (Mozambique), 7/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Anatitengera ku Ukapolo ku Siberia! (V. Kalin), 5/8
Kulera Ana Asanu ndi Aŵiri (B. ndi M. Dickman), 1/8
Kulera Ana mu Afirika (C. McLuckie), 12/8
Kutumikira Mulungu Poyang’anizana ndi Imfa (J. Mancoca), 9/8
Mkango Wobangula Usanduka Mwana wa Nkhosa Wofatsa (E. Torres), 8/8
Mulungu Wakhala Mthandizi Wathu (F. Coana), 7/8
Ndikuthokoza Yehova Kaamba ka Ana Anga Aamuna Asanu (H. Saulsbery), 4/8
Ngakhale Ndili Wakhungu Ndili Wofunika ndi Wachimwemwe (P. Venetsianos), 2/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Ana ndi Ngozi, 10/8
Chithandizo Chopanda Magazi, 3/8
Chiyembekezo kwa Opunduka (kuduka chiŵalo), 6/8
Kodi Kuika Anthu Magazi N’kofunikadi? 9/8
Kodi Moyo Wanu Ukukuvulazani? 7/8
Magazi Amatenda, 7/8
Makemikolo, 1/8
Malo Okuzungulirani—Mmene Amakhudzira Thanzi Lanu, 7/8
Moyo Wautali Komanso Wabwino, 8/8
Msonkhano wa za Opaleshoni Yopanda Magazi (Moscow), 5/8
“Mwana Wanu Ali ndi Matenda a Shuga!” 10/8
Njira Yolimbana ndi TB, 6/8
Okonda Kuothera Dzuŵa—Tetezani Khungu Lanu! 7/8
Vuto la Kadyedwe, 2/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Mankhwala Ophera Tizilombo, 3/8
Mtedza Wotchedwa Tagua, 11/8
Wamkulu Kwambiri, Wamng’ono Kwambiri (agulugufe), 9/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Ana Ali Pavuto, 4/8
Kuopa Nyukiliya, 9/8
Mankhwala Osokoneza Bongo, 11/8
Nkhondo Idzathadi? 10/8
Ukapolo wa Ana, 6/8
Zaka za Zana la 20—Zaka za Kusintha Kwakukulu, 12/8
ZOSIYANASIYANA
Angelo, 12/8
Chinthu Chamtengo Wapatali Kuposa Ndalama, 10/8
Chofalitsa Chokhala ndi Cholinga, 8/8
Kuuluka, 3/8
Linapulumutsa Ndalama za Munthu Wina, 4/8
“Muli Chidziŵitso Chabwino Bwanji!” 9/8
Nyimbo, 10/8
Zikhulupiriro, 11/8
Zovala Zimene Timavala, 2/8