Zamkatimu
March 8, 2001
Kodi Mbiri Yakale Iyenera Kutiphunzitsa Chiyani?
Kodi mbiri yakale ndi yoyeneradi kuiphunzira? Kodi ingatiphunzitse chiyani? Kodi mbiri ya m’Baibulo ndi yothandiza masiku ano?
3 Mbiri Yakale—Kodi Tiyenera Kuikhulupirira?
4 Kodi Zakale Zingatiphunzitsenji?
8 Kodi Baibulo Ndi Mbiri Yodalirika?
11 Kuona Mbalame N’kosangalatsa Kwambiri
16 Ku Namibia Kuli Zoumba Zosunthasuntha
22 Kodi Mukufunikira Inshuwalansi?
26 Inshuwalansi Imene Aliyense Amafunikira
29 ‘Adzasula Malupanga Awo Kukhala Zolimira’—Liti?
32 Anagoma Nawo Chifukwa Amatchula Mfundo Zenizeni
Ziŵerengero Zochititsa Mantha za AIDS! 14
Anthu oposa mamiliyoni 34 ali ndi HIV. Kodi n’chiyani chimene chachititsa kuti ifale?
Kulimbana ndi Matenda Ofoola Thupi 30
Onani mmene Tanya akulimbanira ndi matenda opweteka kwambiri amene amadwala akazi ambiri.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Chithunzi chili pakati penipeni pa chikuto: Franklin D. Roosevelt Library
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Chithunzi: Brett Eloff