Zamkatimu
May 8, 2002
Kodi Dziko Lonse Lingadzakhaledi Pamtendere?
Palibenso chaka china chimene anthu anasoŵapo mtendere monga chaka chatha. Kodi n’zotheka kuti dziko lonse lingadzakhale pamtendere? Ngati n’zotheka, zidzatheka bwanji?
3 Kodi Anali Munthu Wolimbikitsa Nkhondo Kapena Mtendere
9 Si Zongopeka Kuti Dziko Lonse Lidzakhala Pamtendere!
13 Kuteteza Ndiponso Kuletsa Matenda a Kuthamanga kwa Magazi
16 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
N’chifukwa Chiyani Amene Ndimagona Naye M’chipinda Chimodzi Ali Wovuta Kwambiri?
19 Chinthu Chofunika kwa Tonse
21 N’chifukwa Chiyani Anthu Akuchoka M’zipembedzo Zodziŵika Bwino?
24 Kodi “Kupemphera Pawekha” Kungathetse Vutoli?
26 Njira Yabwino Yokukhutiritsani Mwauzimu
30 Kulimbikitsa Amene Akulira Maliro
31 Chakumwa Chokonkha Kukhosi Chochokera ku Chitsamba Chachilendo
32 Buku Limene Lingathandize Kumanga Mabanja
Chakudya Chopatsa Thanzi N’chosasoŵa 10
Munthu akamadya bwino amakhala wathanzi. Kodi muyenera kudya zakudya zotani kuti mukhale athanzi?