Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 8/06 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2006
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Chinthu Chamadzimadzi Chofunika Kwambiri N’chiti?
    Galamukani!—2006
  • Kupulumutsa Moyo ndi Mwazi—Motani?
    Nsanja ya Olonda—1991
  • Mwazi—Wofunika Koposa Kaamba ka Moyo
    Kodi Mwazi Ungapulumutse Motani Moyo Wanu?
  • Kulemekeza Moyo ndi Mwazi Mwaumulungu
    Coonadi Cimene Cimatsogolera ku Moyo Wamuyaya
Onani Zambiri
Galamukani!—2006
g 8/06 tsamba 1-2

Zamkatimu

August 2006

N’chifukwa Chiyani Magazi Ali Ofunika Kwambiri?

Dokotala akhoza kunena kuti magazi ndi ofunika kwambiri chifukwa cha mmene amagwiritsidwira ntchito pochiza odwala. Koma n’chifukwa chiyani madokotala ambiri tsopano safulumira kuika munthu magazi? Kodi n’chiyani kwenikweni chimene chimachititsa magazi kukhala ofunika kwambiri?

3 Kodi Chinthu Chamadzimadzi Chofunika Kwambiri N’chiti?

5 Kodi Kuika Magazi Anthu Odwala Kudzapitirirabe?

10 Kufunika Kwenikweni kwa Magazi

13 Bwato la ku Galileya—Chuma Chochokera M’nthawi za M’Baibulo

16 Mbalame za M’mphepete mwa Nyanja N’zimene Zimauluka Kwambiri Padziko Lonse

19 Zochitika Padzikoli

20 ‘Ndidzadumpha Ngati Nswala’

26 Chikhulupiriro cha Mwana

30 Kuchokera kwa Owerenga

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 “N’labwino Kwabasi!”

Kodi Ndingathandize Bwanji Anthu Amene Akufunika Thandizo? 23

Achinyamata ambiri masiku ano akugwira nawo ntchito yongodzipereka. Kodi n’chiyani chimawalimbikitsa kuchita zimenezi? Ndipo kodi ndi kupatsa kwamtundu wanji kumene kumathandiza kwambiri?

Kodi Anthu Akafa Amasanduka Angelo? 28

Anthu ambiri amakhulupirira zimenezi, koma kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani imeneyi?

[Chithunzi patsamba 2]

Chithunzi chosonyeza zinthu zosiyanasiyana za m’kati mwa magazi. Onani tsamba 8 kuti mumve zambiri

[Mawu a Chithunzi]

Copyright Dennis Kunkel Microscopy, Inc.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena