Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 4/08 tsamba 19-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2008
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Fotokozani chithunzichi
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Kodi Ndani Ali M’gulu la Makolo a Yesu?
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 4/08 tsamba 19-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Fotokozani chithunzichi

1. Pankhani imene yalembedwa pa Mateyo 25:31-46, kodi “Mwana wa munthu” ndani?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Mateyo 16:13-17.

․․․․․

2. N’chiyani chidzachititsa munthu kuweruzidwa kuti ndi nkhosa kapena mbuzi?

․․․․․

3. N’chiyani chidzachitikire nkhosa, nanga n’chiyani chidzachitikire mbuzi?

․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi ndani kwenikweni akunenedwa kuti “abale anga”? Nanga mungatani kuti muwathandize?

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunso awa ndipo tchulani mavesi a m’Baibulo amene akusowa.

TSAMBA 3 Kodi anthu onyodola adzanena kuti chiyani m’masiku otsiriza? 2 Petulo 3:․․․

TSAMBA 7 Kodi chiwonongeko chodzidzimutsa chidzafika panthawi iti? 1 Atesalonika 5:․․․

TSAMBA 20 N’chifukwa chiyani mutu wa banja uyenera kusamalira banja lake mwakuthupi? 1 Timoteyo 5:․․․

TSAMBA 28 Kodi tiyenera kuchita zinthu zonse motani? Aheberi 13:․․․

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

Kodi Ndani Ali M’gulu la Makolo a Yesu?

Zokuthandizani. Werengani malemba amene angakuthandizeni kupeza yankho. Kenako lembani mayina olondola pa mizereyo.

4. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ndine agogo a Abulahamu.

Werengani Genesis 11:24-26.

5. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ndinasamuka ndi banja langa mumzinda wa Uri n’kupita kudziko la Kanani.

Werengani Genesis 11:31.

6. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Yehova anasintha dzina langa chifukwa anati ndidzakhala “atate wa khamu la mitundu.”

Werengani Genesis 17:5.

◼ Mayankho ali patsamba 19

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Yesu.

2. Zimene munthuyo amachitira abale auzimu a Yesu.

3. Nkhosa zidzalandira moyo wosatha koma mbuzi zidzawonongedwa kotheratu.

4. Nahori.—Luka 3:34.

5. Tera.—Luka 3:34.

6. Abulahamu.—Luka 3:34.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena