Zamkatimu
December 2008
N’chifukwa chiyani tili ndi moyo?
Kuyambira kalekale, anthu amafunsa kuti: ‘Kodi tinachokera kuti? N’chifukwa chiyani tili ndi moyo? Kodi moyo wathuwu ukulowera kuti?’ Onani mayankho a mafunso amenewa.
3 N’chifukwa Chiyani Tili ndi Moyo?
6 Chifukwa Chake Tili ndi Moyo
16 Zithunzi Zokongola Kwambiri Zamiyala
22 Chinyengo cha Otsatsa Malonda
23 Nkhono Zokongola Kwambiri za Paua
26 Nyengo Imene Dzuwa Silituluka
30 Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2008
32 Anachira ndi “Buku Lakale Kwambiri”
Kodi Yesu anabadwa mu December? Kodi n’kofunika kudziwa ngati Yesu anabadwadi mu December?
Mmene Moyo Unalili Zinthu Zitasintha Kwambiri ku Korea 12
Werengani za mavuto amene munthu wina anakumana nawo panthawi ya nkhondo ziwiri zoopsa zimene zinawononga kwambiri dziko la Korea ndiponso za nkhani yovuta imene achinyamata ambiri achikoreya akukumana nayo.