Zamkatimu
March 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Kukhulupirira Zoti Kuli Mulungu N’kothandiza Bwanji?
TSAMBA 3 MPAKA 6
12 Kamphepo Kayaziyazi Komanso Dzuwa Ndi Mankhwala
MUNGAONERENSO MAVIDIYO ACHINGELEZI OTSATIRAWA PA WEBUSAITI YATHU
ACHINYAMATA
Onerani vidiyo yachingeleziyi, kuti mumve zomwe achinyamata anzanu ananena pa nkhaniyi, komanso zimene mungachite kuti anthu asamakuchitireni zachipongwe.
(Pitani pamene palembedwa kuti, BIBLE TEACHINGS > TEENAGERS)
ANA
Mungathe kuonetsa ana anu mavidiyo omwe ndi osangalatsa komanso ophunzitsa monga yakuti, Be Neat and Clean.
(Pitani pamene palembedwa kuti, BIBLE TEACHINGS > CHILDREN)