Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
Bukuli ndi la ․․․․․․․․․․․․․․․․
© 2008
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA
Ulamuliro wonse pa buku lino ndi wathu
Ofalitsa
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF SOUTH AFRICA
1 Robert Broom Drive East, Rangeview, Krugersdorp,1739, R.S.A.
Losindikizidwa mu 2012
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Malemba Achiheberi m’buku lino akuchokera m’Baibulo la Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina. Komabe, Chichewa chake tachilemba m’kalembedwe kamakono. Pamene tasonyeza NW ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures—With References. Malemba Achigiriki akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano Lomasulira Malemba Achigiriki Achikhristu, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Maina a achinyamata ena m’bukuli tawasintha
Photo Credits:
Page 165: Woman with firewood: Godo-Foto; European city: © 2003 BiblePlaces.com