Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Imbirani Yehova
“Ndidzaimbira Yehova moyo wanga wonse. Ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wanga nthawi yonse ya moyo wanga.”—SALIMO 104:33
DZINA _______________________
MPINGO _______________________
© 2011
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA
OFALITSA
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF SOUTH AFRICA
1 Robert Broom Drive East, Rangeview, Krugersdorp, 1739, R.S.A.
Losindikizidwa mu 2011
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.