1 Makhalidwe a Yehova
2 Tikuyamikani Yehova
3 “Mulungu Ndiye Chikondi”
4 Tipange Dzina Labwino kwa Mulungu
5 Khristu Ndi Chitsanzo Chathu
6 Pemphero la Mtumiki wa Mulungu
7 Tidzipereke Monga Akhristu
8 Mgonero wa Ambuye
9 Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!
10 “Ine Ndilipo! Nditumizeni”
11 Tikondweretse Mtima wa Yehova
12 Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha
13 Pemphero Loyamikira
14 Zinthu Zonse Zidzakhala Zatsopano
15 Zolengedwa Zimasonyeza Ulemerero wa Yehova
16 Thawirani ku Ufumu wa Mulungu
17 Pitani Patsogolo Mboninu!
18 Chikondi cha Mulungu N’chosatha
19 Mulungu Watilonjeza Paradaiso
20 Dalitsani Msonkhano Wathu!
21 Anthu Achifundo Amakhala Odala
22 “Yehova Ndi M’busa Wanga”
23 Yehova Ndiye Mphamvu Yathu
24 Yang’ananibe Pamphoto!
25 Chizindikiro cha Ophunzira a Khristu
26 Yendani ndi Mulungu!
27 Khalani Kumbali ya Yehova!
28 Nyimbo Yatsopano
29 Yendani ndi Mtima Wosagawanika
30 Ufumu wa Yehova Wayamba Kulamulira
31 Ndife Mboni za Yehova!
32 Khalani Olimba, Osasunthika
33 Musawaope!
34 Zochita Zathu Zizigwirizana ndi Dzina Lathu
35 Tikuthokoza Mulungu Chifukwa cha Kuleza Mtima Kwake
36 “Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi”
37 Malemba Anauziridwa ndi Mulungu
38 Umutulire Yehova Nkhawa Zako
39 Mtendere Wathu Wamtengo Wapatali
40 Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba
41 Lambirani Yehova Muli Achinyamata
42 “Muthandize Ofookawo”
43 Khalani Maso, Limbani, Khalani Amphamvu
44 Tigwire Ntchito Yokolola Mosangalala
45 Pitani Patsogolo
46 Yehova ndi Mfumu Yathu
47 Lalikirani Uthenga Wabwino
48 Timayenda ndi Yehova Tsiku Lililonse!
49 Yehova Ndi Pothawira Pathu
50 Mulungu Anatipatsa Chitsanzo pa Nkhani Yosonyeza Chikondi
51 Timamatire Yehova
52 Tetezani Mtima Wanu
53 Tigwire Ntchito Mogwirizana
54 Tikhale ndi Chikhulupiriro
55 Tidzapeza Moyo Wosatha!
56 Mulungu Imvani Pemphero Langa
57 Kusinkhasinkha kwa Mtima Wanga
58 Pemphero Langa Losonyeza Kudzipereka
59 Tinadzipereka kwa Mulungu!
60 Mulungu Adzakupatsani Mphamvu
61 Mtundu wa Munthu Amene Muyenera Kukhala
62 Kodi Ndife Anthu a Ndani?
63 Tikhale Okhulupirika Nthawi Zonse
64 Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonad
65 “Njira ndi Iyi”
66 Tizitumikira Yehova ndi Moyo Wathu Wonse
67 Muzipemphera kwa Yehova Tsiku Lililonse
68 Pemphero la Munthu Wovutika
69 Ndidziwitseni Njira Zanu
70 “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti”
71 Mphatso Yochokera kwa Mulungu ya Mzimu Woyera
72 Tizisonyeza Chikondi
73 Tizikondana Kwambiri Kuchokera Mumtima
74 Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka
75 Tili ndi Zifukwa Zambiri Zokhalira Osangalala
76 Yehova Ndi Mulungu Wamtendere
77 Muzikhululuka
78 Kuleza Mtima
79 Kukoma Mtima Ndi Khalidwe Lofunika Kwambiri
80 Tizichita Zinthu Zabwino
81 “Tiwonjezereni Chikhulupiriro”
82 Tsanzirani Khristu Pokhala Anthu Ofatsa
83 Tifunika Kukhala Odziletsa
84 “Ndikufuna”
85 Mphoto Yaikulu Yochokera Kwa Yehova
86 Akazi Okhulupirika Ndiponso Alongo Achikhristu
87 Tsopano Ndife Thupi Limodzi
88 Ana Ndi Mphatso Yochokera kwa Mulungu
89 Yehova Akutipempha Mokoma Mtima Kuti: “Mwana Wanga, Khala Wanzeru”
90 Ulemerero Umene Umabwera Chifukwa cha Imvi
91 Atate Wanga, Mulungu Wanga Ndiponso Bwenzi Langa
92 “Lalikira Mawu”
93 “Onetsani Kuwala Kwanu”
94 Timasangalala Ndi Mphatso Iliyonse Imene Mulungu Amatipatsa
95 “Talawani Ndipo Muone Kuti Yehova Ndi Wabwino”
96 Fufuzani Anthu Oyenerera
97 Pitani Patsogolo, Inu Atumiki a Ufumu!
98 Fesani Mbewu za Ufumu
99 Tamandani Mfumu Yatsopano ya Dziko Lapansi
100 Ndife Gulu Lankhondo la Yehova
101 Tilalikire Choonadi cha Ufumu
102 Tiyeni Tiimbe Nyimbo ya Ufumu!
103 “Kunyumba Ndi Nyumba”
104 Tiyeni Tonse Titamande Ya
105 Zakumwamba Zimalengeza Ulemerero wa Mulungu
106 Tikhale pa Ubwenzi ndi Yehova
107 Bwerani Kuphiri la Yehova
108 Tamandani Yehova Chifukwa cha Ufumu Wake
109 Tamandani Woyamba Kubadwa wa Yehova!
110 Ntchito Zodabwitsa za Mulungu
111 Iye Adzaitana
112 Yehova, Mulungu Wamkulu
113 Tikuyamikira Mulungu Kuti Anatipatsa Mawu Ake
114 Buku la Mulungu Ndi Chuma Chamtengo Wapatali
115 Khalani ndi Moyo Wopambana
116 Kuwala Kukuwonjezereka
117 Tiziphunzitsidwa Ndi Yehova
118 Landiranani
119 Bwerani Mudzatsitsimulidwe!
120 Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso
121 Tizilimbikitsana
122 Khamu la Abale
123 Abusa Ndi Mphatso za Amuna
124 Alandireni Bwino
125 Tizigonjera Mokhulupirika Dongosolo la Mulungu Loyendetsera Zinthu
126 Ntchito Imene Tagwira Chifukwa cha Chikondi
127 Malo Odziwika ndi Dzina Lanu
128 Zochitika za Padzikoli Zikusintha
129 Tigwire Mwamphamvu Chiyembekezo Chathu
130 Moyo Ndi Wodabwitsa
131 Yehova Amapereka Chipulumutso
132 Tiimbire Yehova Chifukwa Wapambana
133 Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke
134 Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano
135 Pirirani Mpaka pa Mapeto