Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 103
  • “Kunyumba Ndi Nyumba”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Kunyumba Ndi Nyumba”
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • “Kumka Kunyumba ndi Nyumba”
    Imbirani Yehova Zitamando
  • “Kunyumba ndi Nyumba”
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • N’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova amalalikira kunyumba ndi nyumba?
    Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri
  • Madalitso Amene Amabwera Chifukwa Choyamikira Chikondi cha Yehova—Gawo 1
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2001
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 103

Nyimbo 103

“Kunyumba Ndi Nyumba”

Losindikizidwa

(Machitidwe 20:20)

1. Kunyumba ndi nyumba

Ife timalalikira.

Konsekonse nkhosa za M’lungu

Zikudyetsedwa.

Zoti Ufumu wa M’lungu

Ukulamulira,

Akhristu akufalitsa,

Akulu ndi ana.

2. Khomo ndi khomo

Tinene za chipulumutso,

Dzina la M’lungu aitane,

Apeze moyo.

Adzaitana bwanji

Dzina lomwe sadziwa?

Choncho mumakomo awo

Tidzalilengeza.

3. Khomo ndi khomo

Tiyeni tifalitse mawu.

Asankhe okha kumvera

Kapena kukana.

Koma dzina la Yehova

Tidzalengezabe.

Ndipo potero

Tidzapezadi nkhosa zake.

(Onaninso Mac. 2:21; Aroma 10:14.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena