Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
Bukuli likufotokoza za moyo komanso utumiki umene Yesu anachita. Likufotokozanso kuti anali munthu wotani, zimene anaphunzitsa, zimene anachita komanso zimene ifeyo tingaphunzirepo.
Bukuli sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pawebusaiti yathu ya www.pr418.com/ny.
Malemba onse m’bukuli achokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu January 2025
Chichewa (jy-CN)
© 2015
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA