Zamkatimu
TSAMBA MUTU
GAWO 1—ZIMENE ZINACHITIKA YESU ASANAYAMBE UTUMIKI WAKE
10 1 Mauthenga Awiri Ochokera kwa Mulungu
12 2 Yesu Analemekezedwa Asanabadwe
14 3 Kubadwa kwa Wokonza Njira
16 4 Mariya Anakhala ndi Pakati Asanakwatiwe
18 5 Kodi Yesu Anabadwa Liti Ndipo Anabadwira Kuti?
20 6 Mwana Amene Mulungu Analonjeza
22 7 Okhulupirira Nyenyezi Anapita Kukaona Yesu
26 9 Yesu Anakulira ku Nazareti
28 10 Yosefe ndi Banja Lake Anapita ku Yerusalemu
30 11 Yohane M’batizi Anakonza Njira
GAWO 2—MMENE UTUMIKI WA YESU UNAYAMBIRA
34 12 Zimene Zinachitika Pamene Yesu Ankabatizidwa
36 13 Zimene Yesu Anachita Atayesedwa
38 14 Yesu Anayamba Kupeza Ophunzira
40 15 Chozizwitsa Choyamba Chimene Yesu Anachita
42 16 Yesu Anali Wodzipereka pa Kulambira Mulungu
44 17 Yesu Anaphunzitsa Nikodemo Usiku
46 18 Ntchito ya Yesu Inayamba Kuwonjezeka Kuposa ya Yohane
48 19 Yesu Analalikira Mayi wa ku Samariya
GAWO 3—YESU ANALALIKIRA KWAMBIRI KU GALILEYA
54 20 Chozizwitsa Chachiwiri Chimene Yesu Anachita ku Kana
56 21 Zimene Zinachitika Yesu Ali ku Sunagoge wa ku Nazareti
58 22 Ophunzira 4 Anakhala Asodzi a Anthu
60 23 Yesu Anachita Zozizwitsa Ali ku Kaperenao
62 24 Yesu Analalikira M’madera Ambiri a ku Galileya
64 25 Yesu Anachitira Chifundo Munthu Wakhate N’kumuchiritsa
66 26 “Machimo Ako Akhululukidwa”
70 28 N’chifukwa Chiyani Ophunzira a Yesu Sankasala Kudya?
72 29 Kodi Kunali Kulakwa Kugwira Ntchito Yabwino pa Tsiku la Sabata?
74 30 Kodi Pali Ubale Wotani Pakati pa Yesu ndi Mulungu?
76 31 Anabudula Ngala za Tirigu pa Tsiku la Sabata
78 32 Kodi Malamulo Ankalola Munthu Kuchita Chiyani pa Tsiku la Sabata?
80 33 Ulosi wa Yesaya Unakwaniritsidwa
82 34 Yesu Anasankha Atumwi 12
84 35 Ulaliki Wotchuka wa Paphiri
92 36 Kapitawo wa Asilikali Anasonyeza Kuti Anali ndi Chikhulupiriro
94 37 Yesu Anaukitsa Mwana Wamwamuna wa Mzimayi Wamasiye
96 38 Yohane Ankafuna Kumva Kuchokera kwa Yesu
98 39 Tsoka kwa M’badwo Umene Sunamvere
100 40 Anawaphunzitsa Kukhululukira Ena
102 41 Kodi Yesu Ankazitenga Kuti Mphamvu Zochitira Zozizwitsa?
104 42 Yesu Anadzudzula Afarisi
106 43 Mafanizo Ofotokoza za Ufumu
112 44 Yesu Analetsa Mphepo Yamphamvu Panyanja
114 45 Anatulutsa Ziwanda Zambiri
116 46 Anachira Atagwira Malaya a Yesu
118 47 Kamtsikana Kanakhalanso ndi Moyo
120 48 Yesu Anachita Zozizwitsa Koma Anakanidwa Ngakhale Kwawo ku Nazareti
122 49 Analalikira ku Galileya Komanso Anaphunzitsa Atumwi
124 50 Anawakonzekeretsa Kuti Azilalikira Ngakhale Pamene Akuzunzidwa
126 51 Anaphedwa pa Tsiku Lokondwerera Kubadwa
128 52 Anadyetsa Anthu Masauzande Ambiri ndi Mikate Komanso Nsomba Zochepa
130 53 Wolamulira Amene Akhoza Kulamulira Mphepo Yamphamvu
132 54 Yesu Ndiye “Chakudya Chopatsa Moyo”
134 55 Anthu Ambiri Anakhumudwa ndi Zimene Yesu Ananena
136 56 Kodi Chimaipitsa Munthu N’chiyani?
138 57 Yesu Anachiritsa Mtsikana Komanso Munthu Wogontha
140 58 Anachulukitsa Mikate Komanso Anachenjeza Ophunzira Ake za Zofufumitsa
142 59 Kodi Mwana wa Munthu Ndi Ndani?
144 60 Anaona Ulemelero wa Khristu Atasandulika
146 61 Yesu Anachiritsa Mnyamata Amene Anali ndi Chiwanda
148 62 Kufunika Kokhala Wodzichepetsa
150 63 Zoyenera Kuchita Anthu Akakhumudwitsana Komanso Wina Akachita Tchimo
152 64 Kufunika Kokhululukira Ena
154 65 Yesu Anaphunzitsa Anthu Ena Ali pa Ulendo Wopita ku Yerusalemu
GAWO 4—YESU ANAKALALIKIRA KU YUDEYA CHAKUMAPETO KWA UTUMIKI WAKE
158 66 Zimene Zinachitika Yesu Atapita ku Chikondwerero cha Misasa ku Yerusalemu
160 67 “Palibe Munthu Amene Analankhulapo Ngati Iyeyo”
162 68 Mwana wa Mulungu Ndiye “Kuwala kwa Dziko”
164 69 Kodi Atate Wawo Anali Abulahamu Kapena Mdyerekezi?
166 70 Yesu Anachiritsa Munthu Amene Anabadwa Wosaona
168 71 Afarisi Anatsutsana ndi Munthu Amene Anali Wakhungu
170 72 Yesu Anatumiza Ophunzira 70 Kuti Akalalikire
172 73 Nkhani ya Msamariya Imatithandiza Kudziwa Mnzathu Weniweni
174 74 Zimene Tikuphunzira pa Nkhani Yochereza Alendo Komanso ya Pemphero
176 75 Yesu Ananena Zimene Zimachititsa Munthu Kukhala Wodala
178 76 Anakadya Kunyumba kwa Mfarisi
180 77 Yesu Anapereka Malangizo pa Nkhani ya Chuma
182 78 Woyang’anira Nyumba Wokhulupirika Ayenera Kukhala Wokonzeka
184 79 Ayuda Ankayembekezera Kuwonongedwa
186 80 M’busa Wabwino Komanso Makola Awiri a Nkhosa
188 81 Yesu Si Mulungu Koma Iye ndi Atate Wake Ndi Amodzi
GAWO 5—YESU ANAKALALIKIRA KUM’MAWA KWA YORODANO CHAKUMAPETO KWA UTUMIKI WAKE
192 82 Zimene Zinachitika Pamene Yesu Ankalalikira ku Pereya
194 83 Kuitanira Anthu ku Chakudya
196 84 Kukhala Wophunzira wa Yesu ndi Udindo Waukulu
198 85 Pamakhala Chisangalalo Munthu Wochimwa Akalapa
200 86 Mwana Wotayika Anabwerera
204 87 Muzichita Zinthu Mwanzeru Pokonzekera Zakutsogolo
206 88 Mmene Zinthu Zinasinthira kwa Munthu Wachuma Komanso kwa Lazaro
210 89 Anaphunzitsa ku Pereya Ali pa Ulendo Wopita ku Yudeya
212 90 Yesu Ndi “Kuuka ndi Moyo”
216 92 Pa Anthu 10 Akhate, Mmodzi Anathokoza Yesu
218 93 Mwana wa Munthu Adzaonekera
220 94 Kupemphera Komanso Kudzichepetsa ndi Zinthu Ziwiri Zofunika Kwambiri
222 95 Anawafotokozera Chifukwa Chothetsera Banja Komanso Kuti Azikonda Ana
224 96 Yesu Anayankha Wolamulira Wachinyamata Amene Anali Wolemera
226 97 Fanizo la Anthu Ogwira Ntchito M’munda wa Mpesa
228 98 Atumwi Anasonyezanso Kuti Ankafuna Udindo Wapamwamba
230 99 Yesu Anachiritsa Anthu Akhungu Komanso Anathandiza Zakeyu
232 100 Fanizo la Ndalama 10 za Mina
GAWO 6—ZIMENE YESU ANACHITA KUMAPETO KWA UTUMIKI WAKE
236 101 Yesu Anakadya Chakudya ku Nyumba kwa Simoni ku Betaniya
238 102 Mfumu Inalowa mu Yerusalemu Itakwera pa Bulu
240 103 Yesu Anayeretsanso Kachisi
242 104 Kodi Ayuda Anakhulupirira Yesu Atamva Mulungu Akulankhula?
244 105 Yesu Anagwiritsa Ntchito Mtengo wa Mkuyu Pophunzitsa Anthu za Chikhulupiriro
246 106 Mafanizo Awiri Onena za Munda wa Mpesa
248 107 Mfumu Inaitanira Anthu ku Phwando la Ukwati
250 108 Yesu Analepheretsa Afarisi Kuti Amugwire
252 109 Anadzudzula Atsogoleri Achipembedzo Omwe Ankamutsutsa
254 110 Tsiku Lomaliza Limene Yesu Anapezeka pa Kachisi
256 111 Atumwi Anapempha Chizindikiro
260 112 Fanizo la Anamwali Limatiphunzitsa Kufunika Kokhala Tcheru
262 113 Fanizo la Matalente Limatiphunzitsa Kufunika Kochita Zinthu Mwakhama
264 114 Khristu Akadzayamba Kulamulira Adzaweruza Nkhosa ndi Mbuzi
266 115 Yesu Anachita Mwambo Womaliza wa Pasika
268 116 Anawaphunzitsa Kudzichepetsa pa Pasika Womaliza
270 117 Chakudya Chamadzulo cha Ambuye
272 118 Anakangananso Kuti Wamkulu Ndani
274 119 Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
276 120 Anali Ngati Nthambi Zobala Zipatso Komanso Anali Mabwenzi a Yesu
278 121 “Limbani Mtima Ndaligonjetsa Dziko”
280 122 Pemphero Lomaliza la Yesu Ali M’chipinda Chapamwamba
282 123 Anapemphera Pamene Anali ndi Chisoni Kwambiri
284 124 Khristu Anaperekedwa Kenako Anamangidwa
286 125 Atamugwira Anapita Naye kwa Anasi Kenako kwa Kayafa
288 126 Petulo Anakana Yesu Kunyumba kwa Kayafa
290 127 Khoti la Sanihedirini Linaweruza Mlandu wa Yesu Kenako Anapita Naye kwa Pilato
292 128 Pilato Komanso Herode Sanamupeze Yesu ndi Mlandu
294 129 Pilato Ananena Kuti: “Taonani! Mwamuna Uja Ndi Uyu!”
296 130 Pilato Anapereka Yesu Ndipo Anthu Anamutenga Kuti Akamuphe
298 131 Mfumu Yosalakwa Inavutika Itapachikidwa Pamtengo
300 132 “Ndithudi Munthu Uyu Analidi Mwana wa Mulungu”
302 133 Anakonza Thupi la Yesu ndi Kukaliika M’manda
304 134 M’manda a Yesu Munalibe Kanthu Chifukwa Anali Ataukitsidwa
306 135 Yesu Ataukitsidwa Anaonekera kwa Anthu Ambiri
308 136 Anaonekera M’mbali Mwanyanja ya Galileya
310 137 Anaonekera kwa Anthu Ambiri Mwambo wa Pentekosite Usanachitike
312 138 Khristu Anakhala Kudzanja la Manja la Mulungu
314 139 Yesu Adzabweretsa Paradaiso Kenako Adzamaliza Kugwira Ntchito Imene Anapatsidwa