Lachisanu
‘MULUNGU AMATIPHUNZITSA KUKONDANA’—1 ATESALONIKA 4:9
M’MAWA
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: N’chifukwa Chiyani “Chikondi Sichitha”? (Aroma 8:38, 39; 1 Akorinto 13:1-3, 8, 13)
10:15 NKHANI YOSIYIRANA: Samalani Kuti Musamadalire Zinthu Zimene Zimatha
Chuma (Mateyu 6:24)
Udindo Komanso Kutchuka (Mlaliki 2:16; Aroma 12:16)
Nzeru za Anthu (Aroma 12:1, 2)
Mphamvu Komanso Kukongola (Miyambo 31:30; 1 Petulo 3:3, 4)
11:05 Nyimbo Na. 40 ndi Zilengezo
11:15 KUWERENGA BAIBULO MWASEWERO: Yehova Anapitiriza Kusonyeza Chikondi Chokhulupirika (Genesis 37:1-36; 39:1–47:12)
11:45 Yehova Amakonda Anthu Amene Amakonda Mwana Wake (Mateyu 25:40; Yohane 14:21; 16:27)
12:15 Nyimbo Na. 20 ndi Kupuma
MASANA
1:25 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:35 Nyimbo Na. 107
1:40 NKHANI YOSIYIRANA: Chikondi Chanu Chisathe Ngakhale Kuti . . .
Munakulira M’banja Lopanda Chikondi (Salimo 27:10)
Mukukumana ndi Mavuto Kuntchito (1 Petulo 2:18-20)
Mukukumana ndi Mavuto Kusukulu (1 Timoteyo 4:12)
Mukudwala Matenda Okhalitsa (2 Akorinto 12:9, 10)
Mukuvutika ndi Umphawi (Afilipi 4:12, 13)
Mukutsutsidwa ndi a M’banja Lanu (Mateyu 5:44)
2:50 Nyimbo Na. 141 ndi Zilengezo
3:00 NKHANI YOSIYIRANA: Chilengedwe Chimasonyeza Kuti Yehova Ndi Wachikondi
Kumwamba (Salimo 8:3, 4; 33:6)
Dziko Lapansi (Salimo 37:29; 115:16)
Zomera (Genesis 1:11, 29; 2:9, 15; Machitidwe 14:16, 17)
Zinyama (Genesis 1:27; Mateyu 6:26)
Thupi la Munthu (Salimo 139:14; Mlaliki 3:11)
3:55 “Yehova Amalanga Aliyense Amene Iye Amamukonda” (Aheberi 12:5-11; Salimo 19:7, 8, 11)
4:15 “Valani Chikondi” (Akolose 3:12-14)
4:50 Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero Lomaliza