Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wcg tsamba 184-185
  • Nthawi ya Mesiya Komanso Otsatira Ake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nthawi ya Mesiya Komanso Otsatira Ake
  • Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mariya Mmagadala Anali Ndani?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • “Ambuye Ndawaona Ine!”
    Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Zimene Zinachitika Yesu Asanayambe Utumiki Wake
    Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
  • Kufika kwa Mesiya
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
Onani Zambiri
Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
wcg tsamba 184-185
Banja la Chikhristu la m’nthawi ya atumwi likulalikira bambo ndi mayi wina mumsika womwe muli anthu ambiri. Kumbuyo kwawo kuli kachisi wa ku Yerusalemu.

GAWO 3

Nthawi ya Mesiya Komanso Otsatira Ake

Losindikizidwa

Gawoli likufotokoza zinthu zimene zinachitika mkati mwa zaka pafupifupi 100. Tiyamba ndi kukambirana za namwali wina wa Chiyuda dzina lake Mariya, yemwe anapatsidwa umodzi mwa utumiki wovuta kwambiri umene Yehova anaperekapo kwa munthu wopanda ungwiro. Pomaliza tikambirana zokhudza mtumwi Yohane amene Yesu ankamukonda kwambiri. M’gawoli tikambirananso zitsanzo za anthu omwe anasonyeza kulimba mtima monga Yohane M’batizi, mtumwi Petulo, Mariya wa ku Magadala, Sitefano ndiponso mtumwi Paulo. Mwachitsanzo, anthuwa analimba mtima kuuza ena kuti Yesu ndi Mesiya ngakhale kuti anthu ena sankavomereza zimenezi. Iwo ankatengera chitsanzo cha Yesu komanso ankalalikira uthenga wonena za iye ngakhale kuti anthu ena ankadana nawo komanso kuwazunza.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena