Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wcg tsamba 186-187
  • Gawo 3 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Gawo 3 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
  • Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Zochitika Zikuluzikulu
  • Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu
    Nkhani Zina
  • Gawo 2 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
    Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Nthawi Imene Zinthu Zosiyanasiyana Zinachitika
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
  • Gawo 1 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
    Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
Onani Zambiri
Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
wcg tsamba 186-187

Gawo 3 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika

Losindikizidwa
Tchati chosonyeza nthawi imene anthu otchulidwa m’gawoli anakhala ndi moyo komanso zinthu zikuluzikulu zomwe zinachitika pa moyo wawo.

Nthawi ya Mesiya Komanso Otsatira Ake

MUNTHU

ZAKA

Zekariya

70*–p. 2 B.C.E.

Elizabeti

70*–p. 2 B.C.E.

Mariya (Mayi a Yesu)

20* B.C.E.–p. 33 C.E.

Yosefe

25* B.C.E.–p. 11 C.E.

Yohane M’batizi

2 B.C.E.–32* C.E.

Yesu

2 B.C.E.–33 C.E.

Petulo

5* B.C.E.–p. 64 C.E.

Mariya wa ku Magadala

5* B.C.E.–p. 33 C.E.

Mariya (Mchemwali wake wa Lazaro)

15* B.C.E.–p. 33 C.E.

Sitefano

5* B.C.E.–33/34* C.E.

Paulo (Saulo wa ku Tariso)

3*-65* C.E.

Baranaba

5* B.C.E.–p. 55 C.E.

Maliko

15*–p. 65* C.E.

Mtumwi Yohane

5* B.C.E.–100* C.E.

“p.” akuimira “pambuyo pa”

*Zaka zosatsimikizirika.

Zochitika Zikuluzikulu

332a B.C.E.

ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Girisi

63-30b B.C.E.

ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Roma

Malawi amoto ali pamutu pa amayi atatu a m’nthawi ya atumwi.

33 C.E.

Anthu analandira mzimu woyera pa Pentekosite

Mtumwi Petulo akulalikira kwa Koneliyo.

36 C.E.

Kwa nthawi yoyamba anthu osadulidwa omwe sanali Ayuda anabatizidwa

Mtumwi Mateyu akulemba mpukutu.

41c C.E.

Mateyu analemba buku loyamba la Uthenga Wabwino

Mzinda wa Yerusalemu komanso kachisi wake zikuyaka moto.

70 C.E.

Yerusalemu ndi kachisi wake anawonongedwa

Mtumwi Yohane akulemba mpukutu.

98d C.E.

Anamaliza kulemba Baibulo

a b c d Zaka zosatsimikizirika.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena