Gawo 2 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
Kuyambira Nthawi ya Mafumu Kufika Nthawi Yomanganso Yerusalemu
Ufumu wa Isiraeli Usanagawanike
MUNTHU |
ZAKA |
|---|---|
Samueli |
1180*-1080* B.C.E. |
Yonatani |
1138*-1078* B.C.E. |
Davide |
1107-1037 B.C.E. |
Abigayeli, Natania |
1100*-1000* B.C.E. |
Mefiboseti |
1083*-1000* B.C.E. |
*Zaka zosatsimikizirika.
Ufumu Utagawikana
MUNTHU |
ZAKA |
|---|---|
Yehoyada |
1005*-875* B.C.E. |
Asa |
1000*-937 B.C.E. |
Eliya, Mkazi wamasiye wa ku Zarefatib |
970*-900* B.C.E. |
Elisa |
950*-850* B.C.E. |
Kamtsikana ka ku Isiraeli |
925*-825* B.C.E. |
Hezekiya |
771-716 B.C.E. |
Manase |
728-661 B.C.E. |
Yosiya |
667-628 B.C.E. |
*Zaka zosatsimikizirika.
Kupita ku Ukapolo ku Babulo
MUNTHU |
ZAKA |
|---|---|
Danieli, Hananiya, Misayeli, Azariyac |
635*-535* B.C.E. |
*Zaka zosatsimikizirika.
Aisiraeli Atabwerera ku Yerusalemu
MUNTHU |
ZAKA |
|---|---|
Esitere |
515*-415* B.C.E. |
Nehemiya |
485*-385* B.C.E. |
*Zaka zosatsimikizirika.
Zochitika Zikuluzikulu
1600d B.C.E.
ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Iguputo
1027 B.C.E.
Kachisi wa Solomo anamalizidwa
997 B.C.E.
Ufumu wa Isiraeli unagawikana
Chitadutsa chaka cha 874e B.C.E.
ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Asuri
740 B.C.E.
Asuri anagonjetsa ufumu wa mafuko 10
625 B.C.E.
ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Babulo
607 B.C.E.
Nebukadinezara anawononga Yerusalemu
539 B.C.E.
ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Mediya ndi Perisiya
537 B.C.E.
Ayuda anamasulidwa ku Babulo
515 B.C.E.
Kachisi anamangidwanso ku Yerusalemu
455 B.C.E.
Mpanda wa Yerusalemu unamalizidwa