Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wcg tsamba 104-105
  • Gawo 2 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Gawo 2 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
  • Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Ufumu wa Isiraeli Usanagawanike
  • Ufumu Utagawikana
  • Kupita ku Ukapolo ku Babulo
  • Aisiraeli Atabwerera ku Yerusalemu
  • Zochitika Zikuluzikulu
  • Gawo 3 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
    Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Gawo 1 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
    Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu
    Nkhani Zina
  • Nthawi Imene Zinthu Zosiyanasiyana Zinachitika
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
Onani Zambiri
Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
wcg tsamba 104-105

Gawo 2 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika

Losindikizidwa
Tchati chosonyeza nthawi imene anthu otchulidwa m’Gawo 2 anakhalapo komanso zochitika zapadera zotchulidwa m’Baibulo.

Kuyambira Nthawi ya Mafumu Kufika Nthawi Yomanganso Yerusalemu

Ufumu wa Isiraeli Usanagawanike

MUNTHU

ZAKA

Samueli

1180*-1080* B.C.E.

Yonatani

1138*-1078* B.C.E.

Davide

1107-1037 B.C.E.

Abigayeli, Natania

1100*-1000* B.C.E.

Mefiboseti

1083*-1000* B.C.E.

*Zaka zosatsimikizirika.

Ufumu Utagawikana

MUNTHU

ZAKA

Yehoyada

1005*-875* B.C.E.

Asa

1000*-937 B.C.E.

Eliya, Mkazi wamasiye wa ku Zarefatib

970*-900* B.C.E.

Elisa

950*-850* B.C.E.

Kamtsikana ka ku Isiraeli

925*-825* B.C.E.

Hezekiya

771-716 B.C.E.

Manase

728-661 B.C.E.

Yosiya

667-628 B.C.E.

*Zaka zosatsimikizirika.

Kupita ku Ukapolo ku Babulo

MUNTHU

ZAKA

Danieli, Hananiya, Misayeli, Azariyac

635*-535* B.C.E.

*Zaka zosatsimikizirika.

Aisiraeli Atabwerera ku Yerusalemu

MUNTHU

ZAKA

Esitere

515*-415* B.C.E.

Nehemiya

485*-385* B.C.E.

*Zaka zosatsimikizirika.

Zochitika Zikuluzikulu

1600d B.C.E.

ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Iguputo

Kachisi wa Solomo.

1027 B.C.E.

Kachisi wa Solomo anamalizidwa

Mapu a dziko la Isiraeli litagawidwa kukhala ufumu wakumpoto ndi wakum’mwera.

997 B.C.E.

Ufumu wa Isiraeli unagawikana

Chitadutsa chaka cha 874e B.C.E.

ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Asuri

Msilikali wa Asuri wanyamula mkondo ndipo akuyenda ndi Ayuda omwe akupita nawo ku ukapolo.

740 B.C.E.

Asuri anagonjetsa ufumu wa mafuko 10

625 B.C.E.

ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Babulo

Mabwinja a kachisi wa ku Yerusalemu.

607 B.C.E.

Nebukadinezara anawononga Yerusalemu

539 B.C.E.

ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Mediya ndi Perisiya

Ayuda omwe anali akapolo akuyenda mosangalala.

537 B.C.E.

Ayuda anamasulidwa ku Babulo

Kachisi komanso guwa zomangidwanso.

515 B.C.E.

Kachisi anamangidwanso ku Yerusalemu

Mpanda wa Yerusalemu womangidwanso.

455 B.C.E.

Mpanda wa Yerusalemu unamalizidwa

a b c Mzerewu ukuimira nthawi imene anthu onsewa anakhala ndi moyo

d e Zaka zosatsimikizirika.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena