Gawo 3 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
Nthawi ya Mesiya Komanso Otsatira Ake
MUNTHU |
ZAKA |
|---|---|
Zekariya |
70*–p. 2 B.C.E. |
Elizabeti |
70*–p. 2 B.C.E. |
Mariya (Mayi a Yesu) |
20* B.C.E.–p. 33 C.E. |
Yosefe |
25* B.C.E.–p. 11 C.E. |
Yohane M’batizi |
2 B.C.E.–32* C.E. |
Yesu |
2 B.C.E.–33 C.E. |
Petulo |
5* B.C.E.–p. 64 C.E. |
Mariya wa ku Magadala |
5* B.C.E.–p. 33 C.E. |
Mariya (Mchemwali wake wa Lazaro) |
15* B.C.E.–p. 33 C.E. |
Sitefano |
5* B.C.E.–33/34* C.E. |
Paulo (Saulo wa ku Tariso) |
3*-65* C.E. |
Baranaba |
5* B.C.E.–p. 55 C.E. |
Maliko |
15*–p. 65* C.E. |
Mtumwi Yohane |
5* B.C.E.–100* C.E. |
“p.” akuimira “pambuyo pa”
*Zaka zosatsimikizirika.
Zochitika Zikuluzikulu
332a B.C.E.
ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Girisi
63-30b B.C.E.
ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Roma
33 C.E.
Anthu analandira mzimu woyera pa Pentekosite
36 C.E.
Kwa nthawi yoyamba anthu osadulidwa omwe sanali Ayuda anabatizidwa
41c C.E.
Mateyu analemba buku loyamba la Uthenga Wabwino
70 C.E.
Yerusalemu ndi kachisi wake anawonongedwa
98d C.E.
Anamaliza kulemba Baibulo