Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wcg tsamba 14-15
  • Gawo 1 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Gawo 1 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
  • Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Chigumula Chisanachitike
  • Pambuyo pa Chigumula
  • Nthawi ya Oweruza
  • Zochitika Zikuluzikulu
  • Gawo 2 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
    Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Gawo 3 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
    Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
  • Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu
    Nkhani Zina
  • Nthawi Imene Zinthu Zosiyanasiyana Zinachitika
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
Onani Zambiri
Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
wcg tsamba 14-15

Gawo 1 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika

Losindikizidwa
Tchati chosonyeza nthawi imene anthu otchulidwa m’Gawo 1 anakhalapo komanso zochitika zapadera zotchulidwa m’Baibulo.

Kuyambira Nthawi ya Inoki Kufika Nthawi ya Oweruza

Chigumula Chisanachitike

MUNTHU

ZAKA

Adamu

4026-​3096 B.C.E.

Inoki

3404-​3039 B.C.E.

Nowa

2970-​2020 B.C.E.

Pambuyo pa Chigumula

MUNTHU

ZAKA

Abulahamu

2018-​1843 B.C.E.

Sara

2008-​1881 B.C.E.

Rabeka

1900*-1775* B.C.E.

Yakobo

1858-​1711 B.C.E.

Yosefe

1767-​1657 B.C.E.

Sifira, Puwa, Amuramu, Yokebedi, Miriamua

1645*-1474* B.C.E.

Mose

1593-​1473 B.C.E.

Kalebe

1552-​1450* B.C.E.

Yoswa

1560*-1450* B.C.E.

Rahabi

1500*-1400* B.C.E.

*Zaka zosatsimikizirika.

Nthawi ya Oweruza

MUNTHU

ZAKA

Naomi, Rute, Debora, Baraki, Yaeli, Gidiyoni, Samisoni, Yefita ndi mwana wake wamkazib

1450*-1120* B.C.E.

Samueli

1180*-1080* B.C.E.

*Zaka zosatsimikizirika.

Zochitika Zikuluzikulu

Chingalawa chikuyandama pamadzi osefukira.

2370 B.C.E.

Chigumula chapadziko lonse

Abulahamu akuyang’ana nyenyezi.

1943 B.C.E.

Pangano la Abulahamu linayamba kugwira ntchito

Yakobo ndi banja lake. Chapatali kukuoneka manda a mafumu a ku Iguputo.

1728 B.C.E.

Banja la Yakobo linafika ku Iguputo

1600c B.C.E.

ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Iguputo

Mose wakweza ndodo yake m’mwamba pamene Yehova akugawa madzi a m’Nyanja Yofiira kukhala makoma awiri.

1513 B.C.E.

Ulendo wochoka ku Iguputo

Kalebe ndi Yoswa akuyang’ana Dziko Lolonjezedwa.

1473 B.C.E.

Aisiraeli anafika ku Kanani

Mfumu Sauli.

1117 B.C.E.

Samueli anadzoza Sauli kukhala mfumu

a Mzerewu ukuimira nthawi imene anthu onsewa anakhala ndi moyo.

b Mzerewu ukuimira zaka 330. Munthu aliyense anakhala ndi moyo zaka zosakwana 330 ndipo nthawi imene anabadwa komanso kumwalira sikudziwika.

c Zaka zosatsimikizirika.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena