Mutu wa Bukuli/Tsamba la Ofalitsa
Muziyenda Ndi Mulungu Molimba Mtima
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu pa donate.jw.org.
Malemba onse m’bukuli akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu October 2025
Chichewa (wcg-CN)
© 2025
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania