Zimene Zili M’bukuli
Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira 2
MAWU OYAMBA: Mukhoza Kukhala Olimba Mtima Kwambiri 4
GAWO 1
Kuyambira Nthawi ya Inoki Kufika Nthawi ya Oweruza
MUTU MUNTHU TSAMBA
Kuyambira Nthawi ya Inoki Kufika Nthawi ya Oweruza 12
Gawo 1 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika 14
1 Anayenda Ndi Mulungu Inoki 16
3 Anakana Kumangoganizira Zam’mbuyo Sara 24
4 Munthu Woyamba Kumenya Nkhondo za Yehova Abulahamu 28
5 Anavomera Kuchita Chinthu Chovuta Kwambiri Abulahamu 32
6 Analolera Kusiya Achibale Ake Rabeka 36
7 Analimba Mtima Kuti Ateteze Banja Lake Yakobo 40
8 Sanagonje Atakumana Ndi Mayesero Yosefe 44
9 ‘Chifukwa cha Chikhulupiriro Anabisa Mose’ Sifira, Puwa, Amuramu, Yokebedi, Miriamu 48
10 Anasankha Zinthu Mwanzeru Mose 52
12 Anakhalabe Wokhulupirika kwa Mulungu Wake Kalebe 62
13 Anatsatira Malangizo Achilendo Yoswa 66
14 Anasankha Yehova Kukhala Mulungu Wake Rahabi 70
15 Anathandizana pa Nthawi ya Mavuto Naomi ndi Rute 74
16 “Tipitiradi Limodzi” Baraki ndi Debora 78
17 “Mkazi Wodalitsika Kwambiri” Yaeli 82
18 Anali Wolimba Mtima Komanso Ankachita Zinthu Mosamala Gidiyoni 86
19 Anakwaniritsa Lumbiro Lovuta Yefita ndi Mwana Wake Wamkazi 90
20 Analimba Mtima pa Nthawi Yomwe Anali Wofooka Samisoni 94
21 Mnyamata Amene Analankhula Molimba Mtima Samueli 98
GAWO 2
Kuyambira Nthawi ya Mafumu Kufika Nthawi Yomanganso Yerusalemu
Kuyambira Nthawi ya Mafumu Kufika Nthawi Yomanganso Yerusalemu 102
Gawo 2 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika 104
22 Anafunika Kulimba Mtima Kuti Akhalebe Wokhulupirika Yonatani 106
23 Analimba Mtima Kumenyana Ndi Chimphona Davide 110
24 Ankafunika Kulimbana Ndi Amuna Awiri Okwiya Abigayeli 114
25 Analimba Mtima Kuchita Zoyenera Davide 118
26 Anadzudzula Mfumu Natani 122
27 Sanakhumudwe Pamene Ankachitiridwa Zopanda Chilungamo Mefiboseti 126
28 Anatumikira Yehova Ndi Mtima Wonse “kwa Moyo Wake Wonse” Asa 130
29 “Mulungu Wanga Ndi Yehova” Eliya 134
30 Anasonyeza Kulimba Mtima pa Nthawi Yovuta Kwambiri Mayi Wamasiye wa ku Zarefati 138
31 Kamtsikana Kanalankhula Molimba Mtima Kudziko la Eni Kamtsikana ka ku Isiraeli 142
32 ‘Inu Yehova, Mutseguleni Maso’ Elisa 146
33 Anateteza Mfumu Yosankhidwa ndi Yehova Yehoyada 150
34 “Sanamusiye Yehova” Hezekiya 154
35 Analimba Mtima N’kulapa Manase 158
36 Anathandiza Anthu Kuti Ayambirenso Kulambira Yehova Yosiya 162
38 “Sanapse Ndi Moto” Aheberi Atatu 170
39 “Ngati Nʼkufa, Ndife” Esitere 176
40 Anamanganso Mpanda Nehemiya 180
GAWO 3
Nthawi ya Mesiya Komanso Otsatira Ake
Nthawi ya Mesiya Komanso Otsatira Ake 184
Gawo 3 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika 186
41 “Anali Olungama Pamaso pa Mulungu” Zekariya ndi Elizabeti 188
42 Analimba Mtima N’kuvomera Mariya 192
43 Anali Bambo Wolimba Mtima Yosefe 196
44 ‘Palibe Wamkulu Kuposa Iyeyu’ Yohane M’batizi 200
45 “Ndine Munthu Wochimwa” Petulo 204
46 “Ambuye Ndawaona Ine!” Mariya wa ku Magadala 208
47 “Wachita Zimene Akanatha” Mariya, Mchemwali Wake wa Lazaro 212
48 “Munthu wa Chikhulupiriro Cholimba Ndiponso Wodzaza Ndi Mzimu Woyera” Sitefano 216
49 Anadzakhala Thanthwe Petulo 220
50 Anasintha Kwambiri Maganizo Ake Saulo wa ku Tariso 224
51 “Mwana Wotonthoza” Baranaba 228
52 “Amandithandiza” Maliko 232