Gawo 1 Nthawi Yomwe Zinthu Zinachitika
Kuyambira Nthawi ya Inoki Kufika Nthawi ya Oweruza
Chigumula Chisanachitike
MUNTHU |
ZAKA |
|---|---|
Adamu |
4026-3096 B.C.E. |
Inoki |
3404-3039 B.C.E. |
Nowa |
2970-2020 B.C.E. |
Pambuyo pa Chigumula
MUNTHU |
ZAKA |
|---|---|
Abulahamu |
2018-1843 B.C.E. |
Sara |
2008-1881 B.C.E. |
Rabeka |
1900*-1775* B.C.E. |
Yakobo |
1858-1711 B.C.E. |
Yosefe |
1767-1657 B.C.E. |
Sifira, Puwa, Amuramu, Yokebedi, Miriamua |
1645*-1474* B.C.E. |
Mose |
1593-1473 B.C.E. |
Kalebe |
1552-1450* B.C.E. |
Yoswa |
1560*-1450* B.C.E. |
Rahabi |
1500*-1400* B.C.E. |
*Zaka zosatsimikizirika.
Nthawi ya Oweruza
MUNTHU |
ZAKA |
|---|---|
Naomi, Rute, Debora, Baraki, Yaeli, Gidiyoni, Samisoni, Yefita ndi mwana wake wamkazib |
1450*-1120* B.C.E. |
Samueli |
1180*-1080* B.C.E. |
*Zaka zosatsimikizirika.
Zochitika Zikuluzikulu
2370 B.C.E.
Chigumula chapadziko lonse
1943 B.C.E.
Pangano la Abulahamu linayamba kugwira ntchito
1728 B.C.E.
Banja la Yakobo linafika ku Iguputo
1600c B.C.E.
ULAMULIRO WAMPHAMVU PADZIKO LONSE: Iguputo
1513 B.C.E.
Ulendo wochoka ku Iguputo
1473 B.C.E.
Aisiraeli anafika ku Kanani
1117 B.C.E.
Samueli anadzoza Sauli kukhala mfumu
a Mzerewu ukuimira nthawi imene anthu onsewa anakhala ndi moyo.
b Mzerewu ukuimira zaka 330. Munthu aliyense anakhala ndi moyo zaka zosakwana 330 ndipo nthawi imene anabadwa komanso kumwalira sikudziwika.
c Zaka zosatsimikizirika.