Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • rsg19
  • Chiwerewere

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chiwerewere
  • Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019
  • Timitu
  • Kugonana kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha
  • Kuseweretsa Maliseche
  • Kuonera Zolaula
  • Achinyamata
Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019
rsg19

Chiwerewere

Onaninso mutu wakuti Moyo wa Banja ➤ Mavuto a M’banja ndi Njira Zowathetsera ➤ Chigololo ndiponso mutu wakuti Dziko la Satana ➤ Mzimu wa Dziko ➤ Kuwonjezeka kwa Makhalidwe Oipa

Pa nkhani zokhudza chiwerewere, onani mutu wakuti Dziko la Satana ➤ Kuphwanya Malamulo Ndiponso Zachiwawa

N’zotheka Kukhalabe Oyera Nsanja ya Olonda, 6/15/2015

Zimene Baibulo Limanena: Chigololo Galamukani!, 6/2015

❐ Nsanja ya Olonda, 5/15/2015

Khalani Maso Satana Akufuna Kukumezani

N’zotheka Kugonjetsa Satana

Zimene Baibulo Limanena: Kugonana Musanakwatirane Galamukani!, 9/2013

❐ Nsanja ya Olonda, 11/1/2011

Kodi N’chifukwa Chiyani Kudziwa Zimenezi Kuli Kofunika?

Mayankho a Mafunso 10 Okhudza Kugonana

Kodi N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kutsatira Mfundo za M’Baibulo?

Zimene Baibulo Limanena: Kodi N’kulakwa Mwamuna ndi Mkazi Kukhalira Limodzi Asanakwatirane? Galamukani!, 10/2009

Kodi Mudzasungabe Umphumphu? Nsanja ya Olonda, 12/15/2008 ¶10

Khalani ‘Oyera Poopa Mulungu’ Nsanja ya Olonda, 5/15/2008

“Thawani Dama” ‘Mulungu Apitirize Kukukondani,’ mutu 9

Bwanji Zolumbira Kukhala Odzisunga? Galamukani!, 2/2007

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Ngati Anthu Akukondana Ndiye Kuti Palibe Cholakwika Atagonana Asanakwatirane? Galamukani!, 11/2006

Mafunso Ochokera kwa Owerenga: Kodi munthu angachotsedwe mumpingo wachikhristu chifukwa chochita zodetsa? Nsanja ya Olonda, 7/15/2006

“Kodi Yehova Akufuna Chiyani kwa Iwe?” (Kamutu: Akufuna Kuti Tikhale ndi Makhalidwe Abwino; Kamutu:  Akufuna Kuti Tikhale Oyera) Tsiku la Yehova, mutu 8

Khalanibe Odzisunga mwa Kutchinjiriza Mtima Wanu Nsanja ya Olonda, 2/15/2004

Kodi Luso la Kulingalira Lingakutetezeni Bwanji? Nsanja ya Olonda, 8/15/2002

Musakhale Akumva Oiwala Nsanja ya Olonda, 6/15/2001

Kugonjetsa Kufooka Kwaumunthu Nsanja ya Olonda, 3/15/2001

“Sunga Malangizo Anga, Nukhale ndi Moyo” Nsanja ya Olonda, 11/15/2000

❐ Nsanja ya Olonda, 11/1/2000

Makhalidwe Abwino Akumka Nachepa

Kodi Makhalidwe a M’Baibulo Ndiwo Ali Abwino Koposa?

Lingaliro Laumulungu la Khalidwe Loyera

Mungakhalebe ndi Khalidwe Loyera

Tetezani Dzina Lanu (Kamutu: ‘Usasirire Kukongola Kwake’; Kamutu: ‘Musatenge Moto Pachifuwa Chanu’) Nsanja ya Olonda, 9/15/2000

Mukhoza Kudzisunga M’dziko Lachiwerewereli Nsanja ya Olonda, 7/15/2000

Kugonana kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha

Kodi Baibulo Limalola kuti Akazi Kapena Amuna Okhaokha Azigonana? Galamukani!, Na. 4 2016

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Tiyenera Kuyamba Kuvomereza Khalidwe Logonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha? Galamukani!, 1/2012

Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani Yogonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 23

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani Yogonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha? (Bokosi: Bwanji za Akazi Amene Amagonana ndi Amuna Komanso Akazi Anzawo, Kapena Amuna Amene Amagonana ndi Akazi Komanso Amuna Anzawo?) Galamukani!, 12/2010

Kodi Ndingapewe Bwanji Mtima Wofuna Kugonana ndi Amuna Kapena Akazi Anzanga? Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 28

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndingapewe Bwanji Khalidwe Lofuna Kugonana ndi Amuna Kapena Akazi Anzanga? Galamukani!, 2/2007

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Mulungu Amavomereza Maukwati a Amuna Okhaokha Kapena Akazi Okhaokha? Galamukani!, 4/8/2005

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Mulungu Amavomereza Makhalidwe a Kugonana Kwachilendo? Galamukani!, 10/8/2003

Kodi Muli ndi Vuto Ndinu Kapena Chibadwa Chanu? Nsanja ya Olonda, 6/1/2002

Kuseweretsa Maliseche

Kodi Ndingatani Kuti Ndisiye Chizolowezi Choseweretsa Maliseche? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 25

Mungathe Kuthetsa Vuto Loseweretsa Maliseche ‘Mulungu Apitirize Kukukondani,’ Zakumapeto

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndingathetse Bwanji Chizolowezi Chimenechi? Galamukani!, 11/2006

Kuonera Zolaula

Mungathe Kukana Mayesero Nsanja ya Olonda, 4/1/2014

Kodi Kuonera Zolaula Kuli Ndi Mavuto Otani? Nsanja ya Olonda, 8/1/2013

Zimene Baibulo Limanena: Kuonera Zolaula Galamukani!, 3/2013

Mafunso Ochokera kwa Owerenga: Kodi Mkhristu angachotsedwe mumpingo chifukwa cha chizolowezi choonera zolaula? Nsanja ya Olonda, 3/15/2012

Kodi Mumadana ndi Kusamvera Malamulo? Nsanja ya Olonda, 2/15/2011 ¶10

Musamaone Zinthu Zachabe Nsanja ya Olonda, 4/15/2010 ¶9-11

Khalani “Achangu pa Ntchito Zabwino” (Kamutu: Mverani Machenjezo Mwachangu) Nsanja ya Olonda, 6/15/2009

Chinsinsi cha Banja Losangalala: Khalanibe Okhulupirika Muukwati Wanu Nsanja ya Olonda, 11/1/2008

“Thawani Dama” (Kamutu: Zolaula Zimachititsa Kuti Munthu Achite Dama) ‘Mulungu Apitirize Kukukondani,’ mutu 9

N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupewa Kuona Zithunzi Zolaula? Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 33

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndingapewe Bwanji Kuona Zithunzi Zolaula? Galamukani!, 12/2007

Woipitsa Zinthu Waonekera Ng’amba! (Kamutu: ‘Tchinjirizani Mtima Wanu’) Nsanja ya Olonda, 6/1/2007

Mafunso Ochokera kwa Owerenga: Kodi munthu angachotsedwe mumpingo wachikhristu chifukwa chochita zodetsa? Nsanja ya Olonda, 7/15/2006

❐ Galamukani!, 8/8/2003

Anthu Akusiyana Maganizo pa Zithunzi Zolaula

N’chifukwa Chiyani Zithunzi Zolaula Zatenga Malo?

Zithunzi Zolaula N’zowononga

Zimene Baibulo Limanena: Kodi Kutengeka ndi Zithunzi Zolaula Kulibe Vuto Lililonse? Galamukani!, 7/8/2002

“Khalidwe Lobisika Lowononga Thanzi” Nsanja ya Olonda, 4/15/2001

❐ Galamukani!, 6/8/2000

Zithunzi Zamaliseche Zayamba Kupezeka pa Intaneti

Kodi N’zovulazadi?

Dzitetezeni Nokha Ndiponso Okondedwa Anu

Achinyamata

Kodi Ndingatani Ngati Wina Akundikakamiza Kuti Ndigone Naye? Mayankho a Mafunso 10, funso 7

Kodi Ndiyenera Kudziwa Chiyani Zokhudza Anthu Ogwiririra? Mayankho a Mafunso 10, funso 8

Mfundo Zothandiza Mabanja: Kukambirana ndi Mwana Wanu Nkhani Yotumizirana Zinthu Zolaula Galamukani!, 11/2013

Kodi Kugonana Tili Pachibwenzi Kungachititse Kuti Tizikondana Kwambiri? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 24

Kodi Kugonana Pongofuna Kuthandizana Kuli ndi Vuto? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 26

Kodi Ndingadziteteze Bwanji Kwa Anthu Ogwiririra Anzawo? Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, mutu 32

Kodi Achinyamata Angapeze Bwanji Thandizo? (Kamutu:  Thawani Dama) Galamukani!, 9/2009

Achinyamata, Kumbukirani Mlengi Wanu Wamkulu (Kamutu: Analephera Kulowa Atafika Kale) Nsanja ya Olonda, 4/15/2008

Kodi Tiyenera Kusonyezana Chikondi Mpaka Pati? Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 4

N’chifukwa Chiyani Sindiyenera Kugonana ndi Aliyense Mpaka N’talowa M’banja? Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 5

Kodi Ndingatani Kuti Ndisamangoganiza za Anyamata Kapena Atsikana? Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, mutu 29

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Ndingatani Wina Atandifunsira Kuti Tikagonane? Galamukani!, 3/2007

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndingapewe Bwanji Zogonana Kusukulu? Galamukani!, 3/2006

Vuto Lapadziko Lonse la Atsikana Otenga Mimba Ali Aang’ono Galamukani!, 10/8/2004

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Ndingatani Kuti Ndipewe Kugonana Ndisanalowe M’banja? Galamukani!, 9/8/2004

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Pali Cholakwika Kugonana Tisanakwatirane? Galamukani!, 8/8/2004

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kodi Cholakwika N’chiyani ndi Kugonana kwa pa Telefoni? Galamukani!, 3/8/2004

Zimene Achinyamata Amadzifunsa: Kubereka Ana​—Kodi N’kumene Kumachititsa Mwamuna Kukhala Weniweni? Galamukani!, 5/8/2000

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena