Chosonyezera Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1990
Chosonyeza deti la kope limene nkhaniyo ikupezeka
BAIBULO
Bukhu Lamakedzana la Bezae, 2/15
Bukhu lamakedzana la Washington, 6/1
Kodi mungalikhulupirire Baibulo? 2/1
Kodi Timafunikiradi Oyambirirawo? 7/15
Yohane (Uthenga Wabwino), 3/15
Machitidwe, 5/15, 6/1, 6/15
Aroma 8/1
1 Akorinto, 9/15
2 Akorinto, 9/15
Agalatiya, 11/15
Aefeso, 11/15
Afilipi, 11/15
Akolose, 11/15
CHIDZIŴITSO PA NYUZI
2/15, 3/15, 5/15, 6/15, 7/15, 9/15, 10/15, 11/15, 12/15
LIPOTI LA OLENGEZA UFUMU
1/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 7/1, 8/1, 9/1, 12/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Kodi anthu ambiri oukitsidwa adzakana chowonadi? 3/15
Kodi liwu Lachigiriki lakuti phronema—ndilo “tanthauzo” kapena “kusamalira”? 12/1
Kodi liwu Lachigiriki lakuti pisteuo—ndilo “kukhulupirira” kapena “kusonyeza chikhulupiriro”? 12/1
Kodi majekeseni okhala ndi mbali za mwazi ngolandirika? 6/1
Kodi muyenera kupewa kofi, tiyi? 2/15
Kodi ndiliti pamene malipenga asanu ndi aŵiri anayamba? (Chibv 8-11), 4/1
Kodi njoka “njochenjera”? (Gen 3:1), 10/15
Kodi nkupezekeranji pamaliro? 10/15
Kodi odzozedwa adzapulumuka chisautso chachikulu? 8/15
Kodi Yehova analankhula ndi Adamu mwachindunji? 5/1
Kusaka ndi kusodza, 5/15
MALO KUCHOKERA KU DZIKO LOLONJEZEDWA
Chigwa cha Ela—Kumene Davide Anaphera Chimphona! 1/1
Kodi Mudzaphunzira Kuchokera Kunyengo? 9/1
Kuchokera pa Tabori Kutsikira ku Chilakiko! 5/1
Nazarete—Kwawo kwa Mneneri, 3/1
Samariya—Likulu Pakati pa Malikulu Akumpoto, 11/1
Yordano Amene Simungamdziŵe, 7/1
MBIRI YA MOYO WA ANTHU
Kuchita ndi Zofooka Zanga (T. Addison), 5/1
Kukhulupirira Yehova Kumadzetsa Chimwemwe (J. H. Nathan), 9/1
Kusangalala ndi Kututa mu India (F. E. Skinner), 1/1
Kutumikira Katswiri Wojambula Kuposa Onse, 4/1
Kutumikira Yehova m’Nyengo Yabwino ndi m’Nyengo Yovuta (H. Bently), 6/1
Madalitso A Yehova Andilemeretsa (E. Meynberg), 7/1
Ndaiwona Ikukula Kum’mwera kwa Africa (R. A. McLuckie), 2/1
‘Ndinauluka Pamwamba ndi Mapiko Monga Ziwombankhanga’ (I. Berg), 4/1
Tinalera Ana Asanu ndi Atatu M’chilangizo cha Yehova (O. Menezes), 8/1
Yehova Anadalitsa Kutsimikiza Mtima Kwanga (R. Wuttke), 10/1
Yehova Wandipatsa Nyonga (E. Okoka), 12/1
MBONI ZA YEHOVA
Chifukwa Chake Réunion Ili ndi Nyumba Zaufumu Zambiri, 9/15
Chikristu Chowona Chikuwongolera Moyo m’Sweden, 5/15
Chizunzo Chipitirizabe mu Burundi, 1/1
Chochita Chanzeru Tsoka Lisanakanthe, 7/15
Kuchereza kwa Melita Kudzetsa Madalitso, 7/15
“Kuchirimika Monga Gulu Limodzi Lankhosa” mu Chad, 10/15
Kuchitira Umboni M’malo Abizinezi—Njira Yachijapan, 2/1
Kudzipereka Kwaumulungu—Kopindulitsa Zinthu Zonse (Poland), 1/15
Kufalitsa kwa Padziko Lonse kwa Mbiri Yabwino, 1/1
Kugwa kwa Babulo kufalitsidwa mu Japan, 3/1
Kugwira Ntchito ya Mulungu M’njira ya Mulungu mu Nigeria, 8/15
Kumaliza Maphunziro a Gileadi, 6/1, 12/15
‘Kusodza Anthu’ mu Belize, 4/15
Kututa Zochuluka Kubweretsa Chisangalalo mu Taiwan, 11/15
Lipoti Lautumiki la Chaka, 1/1
Mmene Yehova Amapititsira Patsogolo Ntchito Yake, 12/1
Sierra Leone—“Madiamond” Ake Amtengo Koposa, 3/15
“Tsopano Tiri ndi Nyumba Yaufumu Yathu Yathu,” 5/1
MOYO NDI UMINISITALA ZA YESU
(Nkhani zowonekera m’kope lirilonse.)
MOYO WACHIKRISTU NDI MIKHALIDWE
“Chirimikani”—Musakhumudwe, 4/15
Kodi Mudzapindula ndi Chisomo?, 2/15
Kodi Mumatsatira Malangizo? 10/1
Kodi Nkulondoleranji Chilungamo? 10/15
Kumbukirani Mlengi Wanu Wamkulu Muunyamata Wanu, 5/15
Kusunga Nthaŵi ndi Inu, 6/15
Kuthandiza Ochita Tondovi Kupezanso Chimwemwe, 3/15
Kuwona Mtima Kuli Lamulo Labwino Koposa, 3/1
Lamulirani Mkwiyo Wanu! 9/15
Lemekezani Yehova ndi Chuma Chanu, 7/1
Musanyalanyaze Mnzanu! 8/15
‘Pemphereranani,’ 11/15
Pitirizanibe Kuyenda m’Chowonadi, 9/1
‘Pitirizani Kukhala Wowongolereka,’ 11/1
Tsitsimulani Achibale Anu, 2/15
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRIDWA
Achichepere Achimwemwe mu Utumiki wa Yehova, 8/1
‘Achimwemwe Ali Awo Amene Apirira,’ 1/1
Anthu a Yehova Alimbitsidwa m’Chikhulupiriro, 6/15
‘Chachikulu cha Izi Ndicho Chikondi,’ 11/15
Chikondi Chenicheni Chimafupa, 11/15
Chilungamo Osati Miyambo Yapakamwa, 10/1
Chinsinsi Chopatulika Chivumbuluka, 1/15
Chipulumutso Chiri Pafupi kwa Anthu Odzipereka Mwaumulungu! 4/15
Chiweruzo cha Mulungu Motsutsana Ndi “Munthu Wosayeruzika,” 2/1
Chuma Chathu, Uminisitala Wamakono Waulemerero, 7/15
Dalitsani Dzina Loyera la Yehova! 9/15
Iwo Anachivomereza Chikondi cha Mulungu Mopanda Dyera, 12/1
‘Kapolo Wokhulupirika’ ndi Bungwe Lake Lolamulira, 3/15
Kawonedwe ka Mkristu ka Maulamuliro Aakulu, 11/1
Kawonedwe Kanu ka Moyo kamayambukira Moyo Wanu, 5/1
Khalani Akuchita Mawu, Osati Akumva Okha, 10/1
Khalani Oyamikira—Ufumu Waumesiya wa Yehova Ukulamulira, 10/15
Kodi Mukukalimira? 9/1
Kodi Muli Woyeneretsedwa Kutumikira? 9/1
Kodi Mumayamikira Zimene Mulungu Wachita? 8/1
Kodi Tingavomereze Motani Chikondi cha Mulungu Mopanda Dyera? 12/1
Konzekerani Kaamba ka Chipulumutso Kuloŵa m’Dziko Latsopano, 4/15
Kuchokera ku Seder Kumka ku Chipulumutso, 2/15
Kugonjera Kwathu Kochepa ku Maulamuliro Aakulu, 11/1
Kugwira Ntchito ndi Yehova Mokhulupirika, 8/15
Kugwirizana ndi Bungwe Lolamulira Lerolino, 3/15
Kukhulupirika—Pamtengo Wotani? 8/15
Kuphunzira Chinsinsi Chopatulika cha Kudzipereka Kwaumulungu, 1/15
Kuthetseratu Nkhani ya Chilengedwe Chonse, 7/1
Kuvumbula “Munthu Wosayeruzika,” 2/1
Kuwanditsa Fungo Lokoma la Chidziŵitso Chonena za Mulungu, 7/15
Kuyamikira Chifukwa Chimene Mesiya Ankadzera, 10/15
Kuzindikira “Munthu Wosayeruzika,” 2/1
‘Kuzindikira Zimene Ife Tiri’—Panthawi ya Chikumbutso, 2/15
Lengezani Ufumu wa Yehova Molimba Mtima! 6/15
Limbikitsanani Pamene Tsiku Likuyandikira, 12/15
Londolani Kudzipereka Kwaumulungu Monga Akristu Obatizidwa, 3/1
Mapeto Akudzawo a “Buku la Nkhondo za Yehova,” 7/1
“Mawu a Mulungu Ngamoyo Ndipo Amapereka Mphamvu,” 4/1
Mawu a Mulungu ndi Chowonadi, 4/1
Mawu a Yehova Afalikira! 6/15
Muthange Mwafuna Ufumu ndi chilungamo cha Mulungu, 10/1
Ntchito ya Maulamuliro Aakulu, 11/1
Opani Yehova, Wakumva Pemphero, 5/15
‘Sindichititsidwa Manyazi ndi Mbiri Yabwino,’ 1/1
Sonyezani Chikhulupiriro Kaamba ka Moyo Wosatha, 5/1
“Tiphunzitseni Ife Kupemphera,” 5/15
Tsatirani Chitsanzo cha Yesu cha Kudzipereka Kwaumulungu, 3/1
“Wakumva Anene, Idzani,” 12/15
Yehova Amafunikira Chitamando Chosatha, 9/15
Yehova Ndiye Wolamulira Wathu! 6/1
Yendani M’kuwopa kwa Yehova, 6/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Achichepere Omwe Amatumikira Mulungu, 8/1
“Achimwemwe Ngamtendere,” 8/1
Atumiki Achichepere m’Nthaŵi za Baibulo, 8/1
Armagedo—Liti? 5/15
Betelehemu ndi Krisimasi, 12/15
Chimveni Chowonadi Chonse! 9/15
Chisungiko Chapadziko Lonse—Motani? 6/15
Chuma Chamtengo Woposa wa Golide! 9/15
Dziko Lopanda Umbombo, 2/15
Kodi Adzatsogolera Anthu ku Mtendere Ndani? 4/1
Kodi Amphaŵi Angathe Kukhala Owona Mtima? 11/15
Kodi Kuikidwiratu Kuyenera Kulamulira Moyo Wanu? 8/15
Kodi Moyo Umapulumuka pa Imfa? 9/1
Kodi ndi Mapemphero Andani Amene Amayankhidwa? 1/15
Kodi Ndi Mulungu Uti Amene Mumamlambira? 12/1
Kodi Ndi Mulungu Uti Amene Muyenera Kulambira? 12/1
Kufunafuna Chisungiko, 6/15
‘Kufunafuna Mawu Okondweretsa, Mawu Owongoka,’ 12/15
Kupambana Nkhondo Yolimbana ndi Kuchita Tondovi, 3/1
Kupeza Chimwemwe—Koma Kuti? 3/1
Kusintha Chibadwa cha Anthu, 11/1
Kutembenuzidwa kwa Constantine—Ku Chiyani? 1/15
‘Kutsutsa—Chotchedwa Chidziŵitso Konama’ (Irenaeus), 7/15
Kuwononga Dziko Lapansi, 7/15
“Ligubo Lachigonjetso,” 11/15
Mamiliyoni Amene Ngakufa Tsopano Adzakhalanso Ndi Moyo, 5/1
Masada, 10/15
Mbiri Yabwino Kaamba ka Mtundu Wonse wa Anthu! 1/1
‛Mitembo Yambiri ya Anthu Oyera Mtima inauka,’ 9/1
‘Mkazi Uja Yezebeli,’ 4/1
Mose Wokhala ndi Nyanga—Chopeka cha Mmisiri, 3/15
Mtendere—Kodi Pali Kuthekera Kotani? 4/1
Mtendere wa Dziko Lonse—Kodi Udzatanthauzanjidi? 4/15
Mungapeze Chimwemwe m’Dziko Lochititsa Tondovi! 3/1
Mwala Wachimoabu, 4/15
Nkhondo ya Yeriko—Nthano Kapena Yeniyeni? 7/15
Nthaŵi ya Dziko Latsopano, 10/1
“Pambuyo Pake Anapatsanso Mwamuna Wake,” 6/15
‘Phanga la Achifwamba’ Lamakono, 12/15
Posachedwapa—Dziko Lopanda Zopweteka! 7/15
Tanthauzo la Mwambiwo, 9/15
Umboni wa Ulemerero wa Solomo, 6/15
Yehova Amatidziŵa Bwino! 1/15
Zaka Chikwi Zachitatu—Kodi Zidzakwaniritsa Ziyembekezo Zanu? 6/1
Zaka Chikwi Zopambana Zikuyandikira, 6/1
YEHOVA
Kodi Nchifukwa Ninji Yehova Wavumbula Dzina Lake? 2/15
YESU KRISTU
Kodi Imfa ya Yesu Imatanthauzanji kwa Inu? 3/15