Chosonyezera Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1991
Chosonyeza deti la kope limene nkhaniyo ikupezeka
BAIBULO
Kodi Nlochokera kwa Mulungu? 6/1
Kodi Nlopatulikadi? 6/1
Kusanthula Mbali, 6/15
Mipukutu ya Kunyanja Yakufa, 4/15
New World Translation—Yaukatswiri ndi Yowona, 3/1
1 Atesalonika, 1/15
2 Atesalonika, 1/15
1 Timoteo, 1/15
2 Timoteo, 1/15
Tito, 2/15
Filemoni, 2/15
Ahebri, 2/15
Yakobo, 3/15
1 Petro, 3/15
2 Petro, 3/15
1 Yohane, 4/15
2 Yohane, 4/15
3 Yohane, 4/15
Yuda, 4/15
Chibvumbulutso, 5/1
LIPOTI LA OLENGEZA UFUMU
1/1, 2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 7/1, 8/1, 9/1, 10/1, 11/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Angelo amasonyezedwa ndi mapiko, 3/1
‘Chabwino’ chimene Paulo sanachita (Aroma 7:19), 9/1
Dipo la Yobu (Yobu 33:24), 2/15
Kodi Estere anachita chisembwere ndi mfumu? 1/1
Kodi ‘mmbulu udzakhala kwakanthaŵi ndi mwana wankhosa’? 9/15
Kodi ndiabale auzimu amene akutchulidwa pa Mateyu 10:21? 5/15
Kodi ndiwolemba Baibulo uti anali kazembe wankhondo? 3/15
Kodi ophunzira a pa Yohane 18:15 ndi Marko 14:51, 52 ali ofanana? 4/1
‘Kudziŵa zoweta ziri bwanji’ (Miy. 27:23), 8/1
Kuthira mwazi kolamulidwa ndi khoti, 6/15
Malangizo achipembedzo okakamiza, 12/15
Maluŵa amaliro, 10/15
Nchifukwa ninji panali atumwi okha pa Chikumbutso choyamba? 7/15
29 C.E. deti lofunika, 11/15
Zokometsera, zodzoladzola, 6/1
MBIRI YA MOYO WA ANTHU
‘Amdikira Yehova’ (D. Piccone), 10/1
‘Kubzala ndi Misozi, Kututa ndi Mfuu Yachikondwerero’ (M. Idei), 9/1
‘Kukhala ndi Moyo Tikukumbukira Kuyandikira kwa Tsiku la Yehova’ (L. Reusch), 7/1
Kumamatira Zolimba ku Gulu la Mulungu (R. Ryan), 12/1
Monga Mkazi Wamasiye, Ndinapeza Chitonthozo Chenicheni (L. Arthur), 2/1
Ndiri Nzifukwa Zambiri Chotani Nanga Zokhalira Woyamikira! (L. Hall), 3/1
Nkosangalatsa Kukhala Pagome la Yehova! (E. Wauer), 8/1
Pitirizanibe Kufesa Mbewu—Yehova Adzazikulitsa (F. Metcalfe), 5/1
‘Yehova Ndiye Mulungu Wanga, Amene Ndimkhulupira’ (W. Diehl), 11/1
MBONI ZA YEHOVA
Chimwemwe Chapadziko Lonse, 1/1
Kodi Pali Uminisitala Umene Mungachite? 12/15
Kodi Tingambwezere Motani Yehova? 12/1
Kubweretsa Kuunika Kumalo Akutali a mu Bolivia, 2/15
Kuchitira Umboni m’Falansa—Dziko la Zosiyanasiyana, 6/15
Kufesa Mbewu Zaufumu Kum’mwera kwa Chile, 5/15
Kufunafuna Mulungu kwa Anthu (Bukhu), 4/1
Kulengeza Mbiri Yabwino mu “Mzinda Wachipolynesia” wa ku New Zealand, 3/15
Kulondola Ufulu mu Senegal, 8/15
Kumaliza Maphunziro a Gileadi, 6/1, 12/1
“Kunyumba ndi Nyumba,” 8/1
Kupirira Kwachimwemwe mu Middle East (Lebanon), 1/1
Kututa m’Brazil, 9/15
Mbiri Yabwino Ifika Kumadera Akumidzi a South Africa, 11/15
Misonkhano Yachigawo ya Chinenero Choyera, 1/15
Mtundu Wachimwemwe, 1/1
Soviet Union, 7/15
MOYO NDI UMINISITALA ZA YESU
1/1, 1/15, 2/1, 2/15, 3/1, 3/15, 4/1, 4/15, 5/1, 5/15, 6/1
MOYO WACHIKRISTU NDI MIKHALIDWE
Achichepere—Khalani Olimba m’Chikhulupiriro, 7/15
Achichepere—Kodi Mudzapambana Chiyeso cha Kukhulupirika Kwachikristu? 6/15
Ikani Mulungu Patsogolo m’Moyo Wanu Wabanja! 5/15
Kodi Mumayamikira Gulu Lapadziko Lapansi la Yehova? 11/1
Kodi Mungakondwere ndi Zochita Zambiri? 5/15
Kodi Nchiyani Chimachititsa Chipsinjo m’Banja? 5/15
Kodi Nkuvaliranji Kudzichepetsa? 7/15
Kodi Tingambwezere Motani Yehova? 12/1
Kubwereketsa Ndalama kwa Akristu Anzathu, 10/15
Kugonjera mu Ukwati, 12/15
Kukana Zikhoterero Zauchimo? 8/15
Kumanga Maumunthu Achikristu mwa Ana, 7/1
Kuŵerengera Mtengo Wakusamukira ku Dziko Lokhupuka, 4/1
Mfungulo ya Chikristu Chenicheni, 10/1
“Musakwiyitse Ana Anu,” 10/1
Ntchito ya Mwamuna (Aef. 6:4), 9/1
Otanganitsidwa Kwambiri ndi Mbiri Yabwino, 7/1
“Tiyeninso Tichotse Cholemera Chirichonse,” 10/15
Uminisitala Umene Mungachite? 12/15
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRIDWA
‘Akazi Amene Agwiritsa Ntchito mwa Ambuye,’ 7/1
Chinenero Choyera cha Mitundu Yonse, 4/1
Chipiriro Chimene Chimapeza Chilakiko, 11/1
Chitirani Ulemu Anthu Onse, 2/1
Dalirani Dzanja Lopulumutsa la Yehova, 10/1
Dipo Lolinganira kwa Onse, 2/15
Dzazidwani ndi Chimwemwe, 1/1
Funafunani a Mitima Yowongoka Kaamba ka Moyo Wosatha, 1/15
“Funafunani Mtendere ndi Kuulondola,” 3/1
Gareta Lakumwamba la Yehova Likuyenda, 3/15
Ino Ndiyo Nthaŵi Yakumfuna Yehova, 4/1
Khalani Ogwirizana mwa Chinenero Choyera, 5/1
Khalani Oleza Mtima pa Onse, 5/15
Kodi Mudzatsanzira Chifundo cha Mulungu? 4/15
Kondwerani m’Chiyembekezo cha Ufumu, 12/15
Kudziletsa—Nchifukwa Ninji Kuli Kofunika? 11/15
Kukulitsa Chipatso cha Kudziletsa, 11/15
Kulankhulana m’Banja ndi Mumpingo, 9/1
Kulankhulana Muuminisitala Wachikristu, 9/1
Kulondola Chipembedzo Choyera Kaamba ka Chipulumutso, 12/1
Kumasuka ku Chipembedzo Chonyenga, 12/1
Kupulumutsa Moyo ndi Mwazi—Motani? 6/15
Kuthamanga Makaniwo Mwachipiriro, 11/1
Kutulutsa “Ubwino Wonse,” 8/15
Kutumikira Yehova Mwachimwemwe, 1/1
“Kuunika Kunadza ku Dziko Lapansi,” 8/1
Lankhulani Chinenero Choyera ndi Kukhala ndi Moyo Kosatha! 5/1
Lemekezani Mwanayo, Mtsogoleri Wamkulu wa Yehova, 2/1
Lemekezani Yehova—Chifukwa Ninji Ndipo Motani? 2/1
Lingalirani Zitsanzo za Kuleza Mtima, 5/15
Lolani “Mtendere wa Mulungu” Uchinjirize Mtima Wanu, 3/1
Mbali ya Mkazi m’Malemba, 7/1
Mkondweretseni Yehova Mwakusonyeza Kukoma Mtima, 7/15
“Munagulidwa ndi Mtengo,” 2/15
“Ndithandizeni M’mene Ndisoŵa Chikhulupiriro!” 9/15
Ngachimwemwe Chotani Nanga Ofatsa! 10/15
Nthaŵi Zonse Londolani Kukoma Mtima Kwachikondi, 7/15
Pangani Manja Osatha a Yehova Chichirikizo Chanu, 10/1
Phunzitsani Poyera ndi Kunyumba ndi Nyumba, 1/15
Pitirizani Kuchenjeza za Ntchito Yachilendo ya Yehova, 6/1
Pobisalira Pawo—Bodza! 6/1
Sonyezani Chikhulupiriro Chozikidwa pa Chowonadi, 9/15
Tsanzirani Chifundo cha Mulungu Lerolino, 4/15
Ubwino Waukulu wa Yehova, 8/15
Valani Chifatso! 10/15
“Valani Zida za Kuunika,” 8/1
“Woyang’anira Ayenera Kukhala . . . Wodziletsa,” 11/15
Yandikirani kwa Yehova, 12/15
Yehova ndi Kristu—Olankhula Opambana, 9/1
Yendani Monga Momwe Mwalangizidwa ndi Yehova, 6/15
Yenderani Limodzi ndi Gareta Lakumwamba la Yehova, 3/15
Zidakwa Zauzimu—Kodi Ndizo Yani? 6/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Chipembedzo—Kodi Nchifukwa Ninji Pali Kusoŵeka kwa Chikondwerero? 2/1
Chiweruzo Chomaliza, 8/1
Dziko Latsopano Layandikira! 7/15
Kenturio Wokoma Mtima Wachiroma, 11/15
Kodi Chipembedzo Chirichonse Chiri Chabwinodi? 12/1
Kodi Chipembedzo Nchofunikadi? 12/1
‘Kodi Inali Nthaŵi Yanji?’ 8/1
Kodi Kubwezera Nkolakwa? 11/1
Kodi Mpambuyo Pake Pomwe Simumaganizira? 4/1
Kodi Mtendere Udzabwera Liti? 4/15
Kodi Mtendere Wadziko Lonse Wayandikira? 4/15
Kodi Mtsogolo Ndimolinganizidwa ndi Choikidwiratu? 10/15
Kodi Mulungu Amayankha Mapemphero Anu? 9/15
Kodi Mumalidziŵa Bwino Motani Baibulo? 1/15
Kodi Nchifukwa Ninji Mulungu Waleza Mtima? 10/1
Kodi Ndani Ali ndi Chiitano Chakumwamba? 3/15
Kodi Nkuchitengeranji Mosamalitsa Chipembedzo? 2/1
Kodi Sayansi Ingatsutse Zozizwitsa? 10/1
Kodi Utatu Unaphunzitsidwa ndi Yesu, Ophunzira? 11/1
“Komabe Limayenda!” (Galileo), 12/15
“Korona ndi Bukhu la Umboni,” 2/1
Krisimasi—Kodi Ndiyo Njira Yolandirira Yesu? 12/15
Krisimasi—Nchifukwa Ninji Iri Yotchuka Kwambiri m’Japani? 12/15
Kufikira Mulungu Kovuta, 2/15
Kulaka Upandu, 5/1
Kulambira Mulungu Mayi, 7/1
Kupembedza Zotsala za Akufa, 11/15
Kuulula Machimo, 3/15
Kuuzindikira Mzimu Woyera, 1/15
Lingaliro Labaibulo la Mtendere ndi Chisungiko, 9/1
Mafanizo—Mfungulo ya Kufikira Mitima, 9/15
‘Miliri m’Malo Akuti Akuti,’ 11/15
Mmene Mzimu wa Mulungu Ungakuyambukirireni, 1/15
Ndale Zadziko—Kodi Ziri Mbali ya Ntchito ya Uthenga Wabwino? 4/1
Nkhani Yaikulu, 3/1
Nkhondo Yolimbana ndi Matenda ndi Imfa, 6/15
Posachedwapa Sikudzakhalanso Matenda Kapena Imfa! 6/15
Tanthauzo la Pemphero, 7/15
Thanzi ndi Chimwemwe, 8/15
“Tsiku la Ambuye,” 4/15
Tsiku Lachiweruzo, 8/1
Tsiku Lakubwezera la Mulungu, 11/1
“Udzakhala ndi Ine m’Paradaiso,” 10/15
Upapa—Kodi Unakhazikitsidwa ndi Kristu? 10/15
“Uwu ndi Thupi Langa,” 1/15
Yehova Amamva Kuchonderera Kwathu kwa Thandizo Lamwamsanga, 5/15
YEHOVA
“Ndiye Wankhondo,” 8/15
Yehova ndi Kristu—Olankhula Opambana, 9/1
YESU KRISTU
Dipo—Chiphunzitso Chotaika cha Chikristu Chadziko, 2/15
Kodi Ndimotani Mmene Analiri Mneneri Wofanana ndi Mose? 11/15
Mkangano wa Imfa ya Yesu, 2/15
Mmene Kusandulika Kumakuyambukirirani, 9/15
Yehova ndi Kristu—Olankhula Opambana, 9/1