Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1994
Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo
BAIBULO
Baibulo la Chigothic, 5/15
Buku Loyenera Kuŵerengedwa, 5/15
Kodi Mumaona Baibulo Kukhala Lofunika? 5/15
Lolembedwera Kuti Limvetsetsedwe, 10/1
Phindu Lenileni, 10/1
‘Tsamba Limodzi Lingachotse Mdima Mofanana ndi Nyenyezi,’ 5/15
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Asilikali a Sauli amene anadya nyama ya mwazi, 4/15
Kodi chipatso chimene Hava kenako Adamu anadya chinali apulo? 10/15
Kodi mawuwo, “mnyamata wopanda atate” amasonyeza chisamaliro chochepa pa atsikana? 1/15
Kulandira albumin ya m’mwazi? 10/1
Kulembetsa lamulo la olephera kubweza ngongole, 9/15
Madeti a “nthaŵi zitatu ndi nusu” (Chiv. 11:3), 8/1
‘Uchimo uli kubwatama pakhomo’ (Gen. 4:7), 2/1
Yesu “muzu” wa Jese ndi Davide, 8/15
MBONI ZA YEHOVA
Achichepere Amene ‘Amadalira Yehova,’ 1/1
Apainiya Amapereka ndi Kulandira Madalitso, 1/15
Bahamas, 3/15
Chikhulupiriro Cholimba cha Abale a ku Rwanda, 11/1
Colombia, 7/15
Ethiopia, 8/15
Kodi Nchifukwa Ninji Mboni Zimapitirizabe Kufikira Anthu? 8/15
Kufalitsidwira Pamodzi kwa Zaka Khumi! 4/1
Kumaliza Maphunziro a Gileadi, 6/1, 12/1
Kummaŵa Kugwirizana ndi Kumadzulo, 1/1
Kupenya ndi Chiyamikiro pa “Nyumba ya Mulungu” (Beteli), 6/15
“Kusodza” m’Madzi a Fiji, 6/15
Kuthandiza Okhulupirira mu Bosnia, 11/1
Lipabuliki la Philippines, 1/15
Malaŵi, 5/15
Malire Omalizira a Alaska, 4/15
“Mboni za Yehova Zandichinjiriza!” 5/15
Misonkhano Yachigawo ya “Chiphunzitso Chaumulungu,” 1/15, 7/1, 8/15
Misonkhano Yachigawo ya “Mantha Aumulungu,” 2/15
“Ndasunga Chikhulupiriro” (B. Inconditi), 7/1
Nigeria, 9/15
Othaŵa Kwawo Ali Achimwemwe Kutumikira Mulungu (Central African Republic), 10/15
Poland, 11/15
Thailand, 5/15
Timagulu Totsatira Anthu Kapena Atumiki a Mulungu? 2/15
Tsoka ku Rwanda, 12/15
‘Zochita Zake Zimtsata’ (G. Gangas), 12/1
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Chenjerani ndi Kudzitama, 9/1
Kodi Mukuchita Chifuniro cha Mulungu? 3/1
Kodi Mumathetsa Motani Mikangano? 7/15
Kodi Nkubadi? 4/15
Kodi Ziletso Zimakulefulani? 9/1
Kuleza Mtima, 5/15
Kulimbana ndi Kulakalaka Kumudzi Kwanu, 5/15
Kupima Matenda, 12/15
Kusonyeza Chikondi Chachikristu kwa Okalamba, 8/1
Kusunga Mgwirizano Pakati pa Akulu ndi Atumiki Otumikira, 8/15
Kuthandiza Mwana Wanu Kusankha Yehova, 10/1
Kuŵerengeredwa—Chosoŵa Chachikulu Chachibadwa, 12/1
Laibulale Yateokratiki, 11/1
Lemekezani Ena Popereka Uphungu, 2/1
Magwero a Kulimba Mtima Kosalephera, 9/15
Misonkho, 11/15
Mpikisano, Mfungulo ya Chipambano? 3/1
Musayandikire Pamene Muona Ngozi, 2/15
Nkukhaliranji Wokhululukira? 9/15
Otsimikiza Mtima Kutumikira Yehova! 4/15
Phunziro Laumwini, 6/15
Yamikirani Utumiki Wanu Wopatulika, 9/1
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
“Dzanja la Yehova” m’Moyo Wanga (L. Thompson), 3/1
Dziko Louma Likhala Lachonde (A. Melin), 10/1
Iwo Anatiikira Chitsanzo (C. Zanker), 6/1
Kuchirikizidwa ndi Mulungu Amene Sanganame (M. Willis), 5/1
Kutumikira ndi Gulu Lopita Patsogolo Koposa (R. Hatzfeld), 8/1
Moyo Wolemeretsa, Wofupa mu Utumiki wa Yehova (L. Kallio), 4/1
Ndinapeza Chuma cha Mtengo Wopambana (F. Widdowson), 1/1
Njira ya Moyo ya Chifuno (M. Wieland), 12/1
Tafunafuna Ufumu Choyamba (O. Springate), 2/1
Wachimwemwe mu Ubale Weniweni wa Padziko Lonse (W. Davis), 9/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRIDWA
Abusa ndi Nkhosa m’Teokrase, 1/15
Achichepere—Kodi Mumalabadira Chiphunzitso cha Yani? 5/15
Atumiki a Mulungu—Anthu Olinganizidwa ndi Achimwemwe, 10/1
Chifukwa Chimene Mboni za Yehova Zimakhalira Zodikira, 5/1
Chiphunzitso Chaumulungu Chilakika, 2/1
Chiphunzitso Chaumulungu Chilimbana ndi Ziphunzitso za Ziŵanda, 4/1
Chiphunzitso Chothandiza m’Nthaŵi Zathu Zoŵaŵitsa, 4/15
Chiweruzo cha Yehova pa Aphunzitsi Onama, 3/1
Dalirani Yehova Kuti Adzakwaniritsa Chifuno Chake, 3/15
Gwirani Ntchito Zolimba Kaamba ka Chipulumutso cha Banja Lanu, 7/15
Imbirani Yehova Zitamando, 5/1
Khalani ndi Mtima Wachifundo, 11/1
Kodi Mukudya pa Gome la Yani? 7/1
Kodi Mukukaniza Mzimu wa Dziko? 4/1
Kodi Mumakhululukira Monga Momwe Yehova Amachitira? 10/15
Kodi Mumaphunzitsa Monga Momwe Yesu Anachitira? 10/15
Kodi Mwapeza Chipembedzo Cholondola? 6/1
“Kodi Nchiyani Chidzakhala Chizindikiro cha Kukhalapo Kwanu?” 2/15
Kondwerani mwa Yehova! 9/1
Kuchitira Umboni ku “Mitundu Yonse,” 8/15
Kudziŵa Chipembedzo Cholondola Kumadzetsa Thayo, 6/1
Kugonjera Mwachimwemwe ku Ulamuliro, 7/1
Kulimbana ndi Mphamvu ya Uchimo pa Thupi Lochimwa, 6/15
Kulitsani Mkhalidwe wa Kulolera, 8/1
Kuŵeta Gulu la Mulungu Mwachikondi, 10/1
Lingaliro Lachikristu la Ulamuliro, 7/1
Makolo, Ana Anu Amafunikira Chisamaliro Chapadera, 5/15
Malo Oyenera a Kulambira Yehova m’Miyoyo Yathu, 12/1
Mbiri Yabwino Imeneyi Iyenera Kulalikidwa Choyamba, 8/15
Mlandu wa Yehova ndi Mitundu ya Anthu, 3/1
Mosasamala Kanthu za Kupangidwa ndi Fumbi, Pitanibe Patsogolo! 9/1
Mphotho ya Yobu—Magwero a Chiyembekezo, 11/15
Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!—Magazini Apanthaŵi Yake a Choonadi, 1/1
Ogwirizana m’Chomangira Champhumphu cha Chikondi, 12/15
Olengeza Ufumu Ali Okangalika Padziko Lonse Lapansi, 5/1
Pangani Chiphunzitso Cholamitsa Kukhala Njira Yanu ya Moyo, 6/15
‘Pangani Mabwenzi ndi Chuma Chosalungama,’ 12/1
Pangitsani Ukwati Wanu Kukhala Mgwirizano Wokhalitsa, 7/15
Perekani Chilengezo Chapoyera cha Dzina la Yehova, 9/15
Pezani Mapindu a Chiphunzitso Chaumulungu, 2/1
Tayani Nkhaŵa Yanu Yonse pa Yehova, 11/15
Tengani Chitsanzo cha Aneneri a Mulungu, 9/15
Thaŵirani mwa Yehova, 1/1
“Tiuzeni, Zinthu Izi Zidzachitika Liti?” 2/15
Yehova Alamulira—Kupyolera mwa Teokrase, 1/15
Yehova Ali Wololera! 8/1
Yehova Akhoza Kukulimbikitsani, 12/15
Yehova—Atate Wathu Wodzala Chifundo, 11/1
Yehova—Mulungu wa Chifuno, 3/15
Yendani Monga Olangizidwa ndi Mulungu, 4/15
Yobu Anapirira—Nafenso Tingatero! 11/15
Zipatso—Zabwino ndi Zoipa, 3/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Abrahamu—Woikidwa Panopa, Komabe Wamoyo? 6/15
Akufa Okondedwa—Kodi Tidzawaonanso? 6/15
Anachitidwa Chisomo ndi Yehova (Mariya), 11/15
Anafupidwa Chifukwa Choyenda Mosachimwa (Zakariya, Elisabeti), 7/15
Anazindikira Chikhumbo cha Mtima Wake (Simeoni), 3/15
Chakudya Chamadzulo cha Ambuye—Kangati? 3/15
Chiphunzitso Choikidwa cha Kutengeredwa Kumwamba, 2/15
Chiphunzitso Chokana Mulungu, 12/1
Chisinthiko Chizengedwa Mlandu, 9/1
Chitsogozo Chodalirika, 4/15
Chiwopsezo cha Nyukliya, 8/1
Chiyembekezo kwa Akhungu, 8/15
“Dyetsani Pakamwa, Osati Mapazi” (Miyambo Yamaliro ya mu Afirika), 3/15
Dziko Labwinopo—Loto Chabe? 4/1
Kalenda Yachiyuda, 7/15
‘Kanani Nkhani Zachabe,’ 4/1
Kodi Akufa Ali Kuti? 11/15
Kodi Akufa Amationa? 11/15
Kodi Akufa Angavulaze Amoyo? 10/15
Kodi Chipembedzo Chikukwaniritsa Zosoŵa Zanu? 5/1
Kodi Nchiyani Chachitikira Ulamuliro? 7/1
Kodi Ndimotani Mmene Munthu Angakhalire m’Chifanizo cha Mulungu? 4/1
Kodi Nkhondo Zidzatha Konse? 1/15
Krisimasi—Kodi Ilidi Yachikristu? 12/15
Kufunafuna Chipembedzo Cholondola, 6/1
Kupima Matenda, 12/15
Kusungulumwa, 9/15
Kutsegula Maso Kuti Aone Mbiri Yabwino, 8/15
Kuvutika kwa Anthu—Nchifukwa Ninji Mulungu Wakulola, 11/1
Manda a Petro—Kodi Ali mu Vatican? 10/15
Mantha Akugwira Dziko, 7/15
Mapwando a Tsiku Lakubadwa, 7/15
Mizimu Yoipa, 2/1
Msonkhano Waukulu wa Zipembedzo za Dziko, 2/1
Sanali Wokalamba Kwambiri Kosakhoza Kutumikira Yehova (Anna), 5/15
Sayansi, Chipembedzo, ndi Kufunafuna Choonadi, 9/1
Tchalitchi Chogaŵanika—Kodi Chingapulumuke? 7/1
Timagulu Totsatira Anthu—Kodi Ito Nchiyani? 2/15
Tsoka ku Rwanda, 12/15
William Whiston—Wopanduka Kapena Wophunzira Woona Mtima? 3/15
“Zidziŵa Mawu Ake,” 7/15
Zolemba Zokondweretsa za Josephus, 3/15
OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
1/1, 2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 8/1, 9/1, 10/1
YEHOVA
Kuphunzira kwa Mlangizi Wathu Wamkulu, 9/15
Mawu Ozokota Okhala ndi Tanthauzo Lapadera, 8/15
YESU KRISTU
“Ambuye”—Motani ndipo Liti? 6/1
Kodi Tiyenera Kupemphera kwa Yesu? 12/15
Yesu Anali ndi Chikhulupiriro mwa Mulungu? 10/15