Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1995
Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo
BAIBULO
“Chipangano Chakale” Kapena “Malemba Achihebri”? 3/1
Katswiri Achita Chidwi ndi New World Translation, 4/15
Kodi Baibulo Lili ndi Mtengo Wanji? 3/15
Kodi Malemba a Amasoreti Nchiyani? 5/15
Pamene Amaliŵerenga ndi Mmene Amapindulira 5/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
‘Asakhale aphunzitsi ambiri’ (Yak. 3:1), 9/15
“Dzina limene liposa maina onse” (Afil. 2:9), 11/15
Kodi Afilisti anali ayani? 2/1
Kodi Mulungu anachita tsankhu posankha bungwe lolamulira loyambirira la Ayuda okhaokha? 7/1
Kodi Mariya anali ndi pakati pamene anachezera Elisabeti? 7/15
Kodi Yesu tsopano ndi mkulu wa ansembe kwa “nkhosa zina”? 6/1
“Mbadwo” (1 Pet. 2:9; Mat. 24:34), 11/1
Mkhalidwe wosonyezedwa pa ubatizo, 4/1
“Mulibe mantha m’chikondi” (1 Yoh. 4:18), “opani Mulungu” (1 Pet. 2:17), 8/1
“Mzimu” wa mu Agalatiya 6:8, 6/15
“Nkhosa zina” ndi “khamu lalikulu” pali kusiyana kodi? 4/15
MBONI ZA YEHOVA
Anazichita Kaamba ka Chikondi (nyumba ya mkazi wamasiye ikonzedwa), 10/15
Atene, Greece, 10/15
Brazil, 7/15
Dominican Republic, 2/15
‘Ha, Bwenzi Aliyense Akanakhala Ngati Iwo!’ 9/1
Ife Sitidzapuma pa Ntchito Yathu! (Japan), 3/15
India, 9/15
“Kodi Ndalamazo Zimachokera Kuti?” 12/1
“Kugulitsa Mchere” m’Mozambique, 4/15
Kukwera Phiri Lalitali Kuposa Mapiri a Himalaya (Nepal), 6/15
Kumaliza Maphunziro a Gileadi, 6/1, 12/1
Misonkhano Yachigawo ya “Mantha Aumulungu,” 1/15
“Mkamwa mwa Makanda,” 1/1
Mlandu wa Mboni za Yehova Ugamulidwa (Greece), 12/15
“Ndine Wamtengo Wapatali Pamaso pa Yehova!” 12/15
New Zealand, 11/15
Nyumba ya Ufumu ku Niue, 12/15
Puerto Rico, 1/15
Singapore Apondereza Ufulu wa Kulambira, 10/1
Sri Lanka, 8/15
Sweden, 5/15
Zambia, 3/15
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Chenjerani ndi Kudzilungamitsa! 10/15
Chilungamo Chimakuza Mtundu, 12/15
Chitonthozo cha Awo a “Mtima Wosweka,” 11/1
Kanizani Miyambo Yachikunja! 8/15
Kodi Mungachititse Motani Mapemphero Anu Kukhala Atanthauzo? 3/15
Kodi Mungakulitse Luntha Lowonjezereka? 9/1
Kodi Mungazime Nyali Yofuka? 11/15
Kodi Mwalimbikitsapo Aliyense Posachedwapa? 1/15
Kodi ndi Mlandu wa Yani? 2/1
Kuchotsa—Makonzedwe Achikondi? 7/15
Kuleza Mtima—Nchifukwa Ninji Sikumaonekaoneka? 6/15
Kumvera Kwaumulungu m’Banja la Zipembedzo Zosiyana, 6/1
Kuzindikira Kufooka, Kuipa, ndi Kulapa, 1/1
Mabanja Opembedza Akale, 9/15
Mfupo za Kulimbikira, 8/1
Mmene Akristu Amachitira ndi Chitonzo Chofalitsidwa, 4/1
Mukhoza Kugonjetsa Zopinga Zimenezi! 7/15
‘Musakhale Omangidwa m’Goli Losiyana,’ 11/15
Mzimu Wopatsa, 12/15
Phunziro pa Kusamalira Mavuto, 2/15
Samalirani Changu Chanu, 10/1
Sungani Umphumphu ndi Kukhala ndi Moyo! 1/1
Umbeta m’Nthaŵi za Mavuto a Zachuma, 6/15
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
“Chikondi Sichilephera” (S. Ladesuyi), 9/1
Chinthu Chabwino Koposa Chochita ndi Moyo Wanga (B. Anderson), 3/1
Choloŵa Chathu Chauzimu Chaulemerero (F. Smith), 8/1
Chosankha Changa cha Kufikira Ukulu Msinkhu (C. Dochow), 4/1
Chuma Chosayerekezereka Chogaŵana ndi Ena (G. Malaspina), 1/1
Khama Lichititsa Kupita Patsogolo (J. Maglovsky), 5/1
Kutsatira Mapazi a Makolo Anga (H. Padgett), 10/1
“Popeza Tili Nawo Utumiki. . . . , Sitifooka” (R. Taylor), 2/1
Tinapatsidwa Ngale ya Mtengo Wapatali (R. Gunther), 6/1
Wa Zaka Zana Koma Wolimbabe (R. Mitchell), 12/1
‘Wogwetsedwa, Koma Wosawonongeka’ (U. Helgesson), 11/1
Wokhala Ndekha Koma Wosasiyidwa (A. Lewis), 7/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRIDWA
Akazi Achikristu Ayenera Kuchitiridwa Ulemu, 7/15
“Akuchita Mawu” Achimwemwe, 12/15
Chiitano Chachikondi kwa Otopa, 8/15
Chikondi Chimagonjetsa Nsanje Yoipa, 9/15
Chimwemwe cha Yehova Ndicho Linga Lathu, 1/15
Chitonthozo Chochokera kwa “Mulungu wa Chitonthozo Chonse,” 6/1
Fulumizanani ku Chikondano ndi Ntchito Zabwino—Motani? 4/1
“Goli Langa Lili Lofeŵa, ndi Katundu Wanga Ali Wopepuka,” 8/15
“Israyeli wa Mulungu” ndi “Khamu Lalikulu,” 7/1
Khalani ‘m’Mudzi Wopulumukirako’ Nimukhale ndi Moyo! 11/15
Khamu Lalikulu la Olambira Oona—Lachokera Kuti? 2/1
Khamu Lalikulu Lopereka Utumiki Wopatulika, 2/1
Kodi Mudzaima Motani ku Mpando wa Chiweruzo? 10/15
Kodi Mulungu Ali Pamalo Oyamba m’Banja Lanu? 10/1
Kodi Nchiyani Chimakusonkhezerani Kutumikira Mulungu? 6/15
Kodi Nkhosazo ndi Mbuzizo Zili ndi Mtsogolo Motani? 10/15
Kuchita Mogwirizana ndi Kudzipatulira Kwathu “Tsiku ndi Tsiku,” 3/1
Kudzakhala Kuuka kwa Olungama, 2/15
Kumlaka Satana ndi Ntchito Zake, 1/1
Kuphunzira Kupeza Chisangalalo m’Kuwopa Yehova, 3/15
Kuphunzitsidwa ndi Yehova Mpaka Lero, 8/1
Kupindula ndi Kuŵerenga Baibulo Tsiku ndi Tsiku, 5/1
Kupulumutsidwa Amoyo Kupyola Chisautso Chachikulu, 2/15
Kuŵala kwa Kuunika—Kwakukulu ndi Kwakung’ongo (Mbali 1 ndi 2), 5/15
Kuŵala kwa Kuunika m’Nthaŵi za Atumwi, 5/15
Landirani Baibulo Monga Momwe Lililidi, 5/1
Makolo ndi Ana: Ikani Mulungu Pamalo Oyamba! 10/1
Malo Olemekezeka a Akazi Pakati pa Atumiki a Mulungu Oyambirira, 7/15
Mapindu a Kuwopa Mulungu Woona, 3/15
Mboni Zachikristu Zochirikiza Ulamuliro wa Mulungu, 9/1
Mboni Zachikristu Zokhala ndi Unzika Wakumwamba, 7/1
Mboni Zotsutsa Milungu Yonama, 9/1
Midzi Yopulumukirako—Makonzedwe Achifundo a Mulungu, 11/15
“Momwemo Anachita,” 12/15
Musaleme! 12/1
“Musawopa, Kagulu ka Nkhosa Inu,” 2/15
Mtundu Wosunga Umphumphu, 1/1
Nchifukwa Ninji Tiyenera Kuwopa Mulungu Woona Tsopano? 10/15
Ndinu Wamtengo Wapatali Pamaso pa Mulungu! 4/1
Ngakhale Tilira, Sitili Opanda Chiyembekezo, 6/1
Nsanje ya pa Kulambira Yehova Koyera, 9/15
Nthaŵi ya Kudikira, 11/1
Odzipatulira—Kwa Yani? 3/1
Okhalira Pamodzi mu “Dziko” Lobwezeretsedwa, 7/1
Opulumuka ku “Mbadwo Woipa,” 11/1
Tsiku Lochititsa Mantha la Yehova Lili Pafupi, 4/15
Tsiku “Lotentha Ngati Ng’anjo,” 4/15
Tumikirani Yehova ndi Chimwemwe cha Mtima, 1/15
“Utumiki Wopatulika ndi Mphamvu Yanu ya Kulingalira,” 6/15
Yehova Amapereka Mphamvu kwa Wotopa, 12/1
Yehova—Mulungu Amene Amaphunzitsa, 8/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Aamoni Anabwezera Udani pa Kukoma Mtima, 12/15
Akaraite ndi Kufunafuna Kwawo Choonadi, 7/15
Akathari—Kodi Anali Akristu Ofera Chikhulupiriro? 9/1
Akazi Padziko Lonse, 6/15
Amasoreti, 9/15
Analandira Chitsogozo cha Mulungu (Yosefe, Atate Wolera wa Yesu), 1/15
Anali Kalambula Bwalo wa Mesiya (Yohane Mbatizi), 5/15
Angelo, 11/1
Chipembedzo Chanu—Chombo Chosayenera Kutulukamo? 2/1
Chipembedzo—Kodi ndi Nkhani Yosayenera Kukambitsirana? 4/1
“Choonadi Nchiyani?” 7/1
Chothetsa Nzeru cha Maphunziro a Zaumulungu (Moyo Wosafa), 3/1
Chotupitsa Mkate cha Afarisi ndi Asaduki, 3/15
Dziko Lopanda Kusaona Mtima, 6/1
Dziko Lopanda Nkhondo—Lidzafika Liti? 10/1
Kodi Bizinesi Yanu Idzakutayitsani Chiyani? 5/1
Kodi Choonadi cha Chipembedzo Chingapezeke? 4/15
Kodi Mantha Adzatha Liti? 8/15
Kodi Moyo Ngwamtengo Wapatali Motani kwa Inu? 1/15
Kodi Mudzatamanda Yehova? 3/15
Kodi Mulungu Amalamulira Dziko? 7/15
Kodi Mulungu Anaikiratu za Mtsogolo Mwathu? 2/15
Kodi Udani Udzatha Konse? 6/15
Kuikiratu za Mtsogolo, 2/15
Kuthira Mwazi Kupendedwanso, 8/1
Kuunika Kwawo Sikunazime, 11/15
Luntha la Kulenga—Mphatso Yochokera kwa Mulungu, 2/1
Maimonides—Munthu Amene Anamveketsanso Chiyuda, 3/1
Mantha—Bwenzi Kapena Mdani? 10/15
Mantha—Ofala Tsopano Koma Osati Kwamuyaya! 10/15
Milungu Yachikazi ya Kubala ndi ya Nkhondo, 11/15
Moyo Wabwino Kwambiri Posachedwapa! 11/15
Moyo Watsopano wa Makolo Athu Akufa, 5/15
Munthu Wanjiru, 9/15
Mwambo Wopanda Tanthauzo? (Kuulula Machimo), 9/15
Njira ya ku Ufulu, 9/1
Nsanje, 9/15
Nsanje Inatsala Pang’ono Kuwononga Moyo Wanga, 9/15
Nthaŵi Zabwinopo Mtsogolo, 8/1
Olamulira Okhala m’Malo a Mizimu, 7/15
Pamene Mwambo Uwombana ndi Choonadi, 12/1
Pamene Sikudzakhalanso Mmphaŵi, 5/1
Phiri Limene “Limayenda,” (Ireland), 4/15
William Tyndale—Munthu Woona Patali, 11/15
Wosindikiza Amene Anasiya Chizindikiro Chake (Robert Estienne), 4/15
Zaka Makumi Asanu za Kuyesayesa Kosaphula Kanthu (United Nations), 10/1
OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
1/1, 2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 7/1, 8/1, 9/1, 11/1, 12/1
YEHOVA
Ndalama Zimene Zili ndi Dzina la Mulungu, 5/15
YESU KRISTU
Kodi Kukayikira za Yesu Kuli Koyenera? 8/15
Zozizwitsa za Yesu, 3/1