Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1998
Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo
ANACHITA CHIFUNIRO CHA YEHOVA
Eliya Atamanda Mulungu Woona, 1/1
Paulo Achitira Umboni Molimba Mtima, 9/1
Msamariya Mnansi Wabwino, 7/1
Yesu Anacheza ndi Ana, 11/1
Yesu Atumiza Ophunzira 70, 3/1
Yobu Afupidwa Chifukwa Chokhulupirika, 5/1
BAIBULO
“Baibulo la Chala Chimodzi,” 3/15
Baibulo Latsopano m’Chigiriki Chamakono, 9/1
“Interlinear ya Chipangano Chatsopano Yabwino Koposa,” 2/1
Katswiri wa Maphunziro Asintha Deti la Malembo a Pamanja, 12/15
Kodi Mungalikhulupirire Baibulo? 10/15
Matembenuzidwe a Baibulo Amene Anasintha Dziko Lapansi (Septuagint), 9/15
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Atumwi alephera kuchiritsa mnyamata (Mat. 17:20; Marko 9:29), 8/1
Kukumbukira masiku a ukwati, masiku akubadwa, 10/15
Luka 13:24, 6/15
MBONI ZA YEHOVA
Agamula Kuti Munthu Azidzisankhira (Japan), 12/15
Akapolo a Anthu Kapena Atumiki a Mulungu? 3/15
Baibulo Latsopano m’Chigiriki Chamakono, 9/1
Bolosha la Buku la Anthu Onse, 4/1
“Chitsanzo cha Umodzi ndi Ubale,” 7/15
Chochitika Chosaiŵalika ku France, 7/1
“Gwiritsitsani Chimene Muli Nacho” (Greece), 9/1
Kufikira Ochulukirapo ndi Uthenga Wabwino, 2/15
Kumaliza Maphunziro a Gileadi, 6/1, 12/1
Kuteteza Uthenga Wabwino Mwalamulo, 12/1
Madokotala, Oweruza, ndi Mboni za Yehova, 3/1
Mitima Yonga Mwala Imvetsera (Poland), 10/15
“Mulungu Akonda Wopereka Mokondwera” (zopereka), 11/1
Msonkhano Wachigawo wa “Njira ya Moyo ya Mulungu,” 2/15, 6/1
Nsanjika za Mumzinda Kumka ku Chipululu cha Tundra (Canada), 4/15
Ntchito ‘Yoyeneradi Kulemekezedwa’ (Italy), 8/15
Ntchito Zachikristu Pakati pa Chipwirikiti, 1/15
Pafupi ndi Volokano (Mexico), 8/15
Ukwati Wapadera Kwambiri (Mozambique), 6/15
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Alemekezeni, 4/1
Chenjerani ndi Chisimoni! 11/15
Ikani Zinthu Zofunika Pamalo Oyamba! 9/1
Luso la Kukopa, 5/15
Khalani ndi Moyo Wopindulitsa, 8/15
Kukonzeratu Tsogolo la Okondedwa Athu, 1/15
Kukwaniritsa Udindo wa Kusamalira Banja, 6/1
Kutengapo Phunziro pa Zolakwa Zakale, 7/1
Kuthetsa Mavuto Mwamtendere, 11/1
Kuyamikira Mwayi wa Utumiki Wopatulika, 8/1
Kuyamikira, 2/15
Makolo Tetezerani Ana Anu! 2/15
Malowolo, 9/15
Miyambo ya Maliro, 7/15
Miyambo ya m’Madera ndi Mapulinsipulo Achikristu, 10/1
“Mtima Womvera,” 7/15
Mungapite Patsogolo Mwauzimu, 5/15
Nchitamando Kapena Kusyasyalika? 2/1
Ndipemphe Ngongole kwa Mbale? 11/15
Pitanibe Patsogolo Mwauzimu! 10/1
Tetezerani Ana Anu, 7/15
Mumayamikira Madalitso a Yehova? 1/1
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Chachikulu Chimene Ndimafuna Ndicho Kukondweretsa Yehova (T. Neros), 11/1
“Chifundo Chanu Chiposa Moyo” (C. H. Holmes), 2/1
Kulibe Chinthu Chabwino Choposa Choonadi (G. N. Van der Bijl), 1/1
Kusintha Gawo la Utumiki Pausinkhu wa Zaka 80 (G. Matthews), 5/1
Kusiya Kulambira Mfumu ndi Kuyamba Kulambira Koona (I. Sugiura), 12/1
Kuyamikira Choloŵa Cholimba Chachikristu (G. Gooch), 3/1
Ndinachirimika Paziyeso Zoopsa (É. Josefsson), 6/1
Ndinapeza Chinthu Choposa Golidi (C. Mylton), 10/1
Ndinaphunzira Kudalira Yehova (J. Korpa-Ondo), 9/1
Moyo Wanga Monga Wakhate (I. Adagbona), 4/1
“Tangochita Zimene Tayenera Kuzichita” (G. Couch), 8/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
“Akufa Adzaukitsidwa,” 7/1
Anadedwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo, 12/1
Apereka Chiweruzo m’Chigwa Chotsirizira Mlandu, 5/1
Buku la Anthu Onse, 4/1
Buku Lochokera kwa Mulungu, 4/1
Chenjerani ndi Kusakhulupirira, 7/15
Chikhulupiriro Chachikristu Chidzayesedwa, 5/15
Chikhulupiriro ndi Mtsogolo Mwanu, 4/15
Chipulumutso ncha Yehova, 12/15
Gulu la Yehova Limachirikiza Utumiki Wanu, 6/15
Gwiranibe Ntchito Yake ya Chipulumutso Chanu! 11/1
Khalani Otetezereka m’Gulu Lolinganizidwa la Mulungu, 9/1
Khalanibe m’Teokrase, 9/1
Kodi ‘Adzapulumuka Ndani’? 5/1
Kodi Chikhulupiriro Chanu cha Chiukiriro Ncholimba Motani? 7/1
Kodi Mumalidziŵa Bwino Gulu la Yehova? 6/15
Kodi Mwaloŵa Mpumulo wa Mulungu? 7/15
Kodi Ntchito Yanu Idzapulumuka Moto? 11/1
Kukhala Mogwirizana ndi Kudzipatulira Kwachikristu mu Ufulu, 3/15
Kulimbitsa Chidaliro Chathu mwa Chilungamo cha Mulungu, 8/15
Kupatulidwa ndi Ufulu wa Kusankha, 3/15
Kutchinjiriza Chikhulupiriro Chathu, 12/1
Kuyamikira Misonkhano Yachikristu, 3/1
“Kuyembekezera Mwachidwi” 9/15
‘Kuyenda mwa Chikhulupiriro Osati mwa Chionekedwe,’ 1/15
Kuyenda ndi Mulungu—Masitepe Oyambirira, 11/15
Kuyenda ndi Mulungu—Tikumadikira Umuyaya, 11/15
Lino Ndilo Tsiku la Chipulumutso! 12/15
Madalitso Aakulu Kudzera m’Pangano Latsopano, 2/1
Madyerero Osaiŵalika a m’Mbiri ya Israyeli, 3/1
“Mtima Wako Ngwowongoka Kodi?” 1/1
Mtundu wa Chikhulupiriro Chanu Ukuyesedwa Tsopano, 5/15
“Mulimbanetu Chifukwa cha Chikhulupiriro”! 6/1
Musaleme Kuthamanga Makani a Moyo! 1/1
Nkhosa Zina ndi Pangano Latsopano, 2/1
Nthaŵi ndi Nyengo Zili m’Manja mwa Yehova, 9/15
‘Pitirizani Kuyenda Mogwirizana ndi Kristu,’ 6/1
Pitirizani Kuyenda ndi Mulungu, 1/15
Tiyenera Kudalira Yehova, 8/15
Tsanzirani Yehova—Chitani Chilungamo, 8/1
Tsanzirani Chifundo cha Yehova, 10/1
Tsiku la Yehova Layandikira, 5/1
Ufulu Waulemerero Posachedwapa kwa Ana a Mulungu, 2/15
Yehova Atenga Ana Ambiri Aloŵe Ulemerero, 2/15
Yehova Akwaniritsa Malonjezo Ake kwa Okhulupirika, 4/15
Yehova—Gwero la Chilungamo Chenicheni, 8/1
Yerusalemu—Kodi Ndiye ‘Woposa Chimwemwe Chanu Chopambana’? 10/15
“Yehova, Mulungu Wachifundo ndi Wachisomo,” 10/1
Yehova ndi Mulungu Wamapangano, 2/1
Yerusalemu—“Mzinda wa Mfumu Yaikulukulu,” 10/15
Yerusalemu Woyenereradi Dzina Lake, 10/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Agora—Pachimake pa Atene Wakale, 7/15
Akusiyiranji Chipembedzo? 7/1
Amakabe, 11/15
Anapanga Zonsezi Ndani? 5/1
Anthu “Akumva Zomwezi Tizimva Ife” 3/1
Atcheru ndi Zochitika za m’Nthaŵi Yathu? 9/15
Atsogoleri Achipembedzo Amakhulupirira Zimene Amaphunzitsa? 10/15
Ayuganoti, 8/15
Banja—Lili Pangozi! 4/1
Barnaba—“Mwana wa Chitonthozo,” 4/15
Beteli—Mzinda wa Zabwino ndi Zoipa, 9/1
Bwanamkubwa Wonyada (Belisazara), 9/15
Chenjerani ndi Onyoza! 6/1
Chikumbumtima Chanu Mungachikhulupirire? 9/1
Chilungamo Chenicheni—Liti Ndipo Motani? 6/15
Chilungamo kwa Onse, 8/1
Chisalungamo Sichidzatha? 8/1
Chuma Chingakupatseni Chimwemwe? 5/15
“Choonadi Chidzakumasulani,” 10/1
Choonadi Chimasanduliza Miyoyo, 1/1
Constantine Wamkulu, 3/15
Dariyo, 11/15
Dikirani Moleza Mtima, 6/1
Dziko Lapansi—Kodi Linakhaliraponji? 6/15
Dziko Lapansi Lidzawonongedwa? 6/15
Filemoni ndi Onesimo, 1/15
Khirisimasi Yanyalanyaza Kristu? 12/15
Kodi Tidzafunikira Magulu Ankhondo Nthaŵi Zonse? 4/15
Kulambira Mulungu m’Choonadi, 10/1
Kusadalirana, 8/15
Kusiyanitsa Chabwino ndi Choipa? 9/1
Mariya Anafa Imfa Yachibadwa? 8/1
Mmene Angelo Angakuthandizireni, 11/15
Mphatso Yachikoka—Kodi Munthu Atamandidwe Kapena Mulungu Alemekezedwe? 2/15
Ndinu Woyembekezera Zabwino Kapena Zoipa? 2/1
Pamene Mbala Zamfuti Zikuloŵerani, 12/15
‘Pangani Ophunzira mwa Anthu a Mitundu Yonse,’ 1/1
Sanadzipangire Dzina, 3/15
Talmud, 5/15
Tito, 11/15
Tsogolo Lathu Linalembedweratu? 4/15
Tukiko, 7/15
Yunike ndi Loisi, 5/15
Zipembedzo Zikupepesa, 3/1
OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
2/1, 3/1, 4/1, 6/1, 7/1, 8/1, 10/1, 11/1
YEHOVA
Ali Weniweni kwa Inu? 9/15
Kodi Yehova Ndani? 5/1
YESU KRISTU
Kubadwa Kwake, 12/15
Masiku Omaliza Padziko, 3/15
Maziko a Chikhulupiriro Chenicheni, 12/1
Wolamulira Yemwe “Matulukiro Ake Ndiwo Akale Lomwe,” 6/15