Zamkatimu
June 15, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
MAGAZINI YOPHUNZIRA
AUGUST 5-11, 2013
Makhalidwe a Yehova Ndi Amtengo Wapatali
TSAMBA 7 • NYIMBO: 69, 89
AUGUST 12-18, 2013
Yehova Ndi Wowolowa Manja Ndiponso Wololera
TSAMBA 12 • NYIMBO: 22, 110
AUGUST 19-25, 2013
Yehova Ndi Wokhulupirika Ndiponso Amakhululuka
TSAMBA 17 • NYIMBO: 63, 77
AUGUST 26, 2013–SEPTEMBER 1, 2013
Lolani Kuti Yehova Azikuumbani ndi Malangizo Ake
TSAMBA 24 • NYIMBO: 120, 64
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Makhalidwe a Yehova Ndi Amtengo Wapatali
▪ Yehova Ndi Wowolowa Manja Ndiponso Wololera
▪ Yehova Ndi Wokhulupirika Ndiponso Amakhululuka
Akhristufe timadziwa kuti Yehova ali ndi makhalidwe akuluakulu anayi. Koma nkhani zitatuzi zitithandiza kuona kuti makhalidwe enanso a Yehova amene sitikambiranakambirana ndi amtengo wapatali kwambiri. Tikambirana mmene Yehova amasonyezera khalidwe lililonse ndiponso zimene tingachite kuti timutsanzire.
▪ Lolani Kuti Yehova Azikuumbani ndi Malangizo Ake
Pofotokoza mphamvu imene Yehova ali nayo pa anthufe, Malemba amanena kuti iye ali ngati “Wotiumba.” (Yes. 64:8) Nkhaniyi ikusonyeza kuti tingaphunzire zambiri zokhudza Yehova poona mmene iye ankaumbira anthu m’mbuyomo. Ikufotokozanso mmene iye amatithandizira akamatiumba masiku ano.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 Ndadalitsidwa Kwambiri Chifukwa Chomvera Yehova
22 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
29 Akulu, Kodi Mumalimbikitsa Anthu ‘Olefuka’?
PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira mumsewu mumzinda wa Frankfurt ku Germany
GERMANY
KULI ANTHU
81,751,600
KULI MBONI
162,705
MAPHUNZIRO A BAIBULO
74,466
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO
265,407