Zamkatimu
October 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
DECEMBER 1-7, 2014
Tizikhulupirira Kwambiri Ufumu wa Mulungu
TSAMBA 7 • NYIMBO: 108, 129
DECEMBER 8-14, 2014
TSAMBA 13 • NYIMBO: 98, 102
DECEMBER 15-21, 2014
Kodi Mumayamikira Mwayi Wogwira Ntchito ndi Yehova?
TSAMBA 23 • NYIMBO: 120, 44
DECEMBER 22-28, 2014
“Ikani Maganizo Anu pa Zinthu Zakumwamba”
TSAMBA 28 • NYIMBO: 70, 57
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Tizikhulupirira Kwambiri Ufumu wa Mulungu
▪ ‘Mudzakhala Ufumu wa Ansembe’
Mulungu akugwiritsa ntchito Ufumu wa Mesiya pokwaniritsa cholinga chake padzikoli. M’nkhanizi tiona mapangano angapo amene akukhudza Ufumuwu komanso zifukwa zotichititsa kuukhulupirira kwambiri.
▪ Kodi Mumayamikira Mwayi Wogwira Ntchito ndi Yehova?
Nkhaniyi ikufotokoza za atumiki a Yehova akale komanso a masiku ano. Itithandiza kuti tiziyamikira kwambiri mwayi wogwira ntchito ndi Mulungu.
▪ “Ikani Maganizo Anu pa Zinthu Zakumwamba”
M’masiku otsiriza ano, pali zinthu zambiri zimene zingasokoneze chikhulupiriro chathu. Panalinso zinthu zimene zikanasokoneza chikhulupiriro cha Abulahamu ndi Mose. Kodi tikuphunzira chiyani kwa anthu awiriwa? Nkhaniyi itithandiza kuti tipirire chifukwa itilimbikitsa kuganizira kwambiri za Yehova Mulungu ndi Ufumu wake.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
PATSAMBA LOYAMBA: Alongo awiri akulalikira mumsewu pafupi ndi mapiri enaake, m’tauni ya Tausa kudera la Taita
KENYA
KULI ANTHU
44,250,000
KULI OFALITSA
26,060
MAPHUNZIRO A BAIBULO
43,034
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO MU 2013
60,166