Magazini Yophunzira
August 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: OCTOBER 1-28, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
MALAWI
Woyang’anira dera ndi mkazi wake akonzeka kuti akachezere mpingo wina. Atenga mabuku, pulojekita, zokuzira mawu komanso zinthu zina panjinga
KULI OFALITSA
93,412
MAPHUNZIRO A BAIBULO
145,504
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2017)
315,784
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.