Zilengezo
◼ Mabuku ogwiritsira ntchito mu May: Sabusikripishoni ya Nsanja ya Olonda. June: Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu? July ndi August: Lililonse la mabrosha otsatirawa a masamba 32 lingagwiritsiridwe ntchito: Boma Limene Lidzabweretsa Paradaiso, Dzina la Mulungu Limene Lidzakhala Kosatha, Kodi Chifuno cha Moyo Nchiyani?, Kodi Mulungu Amatisamaliradi?, Kodi Muyenera Kukhulupirira Utatu?, Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, Sangalalani ndi Moyo pa Dziko Lapansi Kosatha!, ndi “Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano.” CHIDZIŴITSO: Mipingo imene sinaodebe zinthu zamkupiti zotchulidwa pamwambapa iyenera kutero pa fomu yawo ya Literature Request (S-AB-14) yotsatira ya mwezi ndi mwezi.
◼ Zofalitsa Zomwe Zilipo:
Chicheŵa: Kalenda ya Mboni za Yehova ya 1995. Chingelezi: Kalenda ya Mboni za Yehova ya 1995; 1995 Yearbook of Jehovah’s Witnesses.