Kodi Mudzapezekapo?
Kupezeka kuti? Ku Msonkhano Wachigawo wa 1999 wa “Mawu Aulosi a Mulungu.” M’Malaŵi mudzakhala misonkhano yachigawo 15. Idzayamba pa August 6 ndipo idzachitika kwa milungu inayi yotsatizana. Ngakhale kuti yambiri idzakhala m’Chicheŵa, idzakhalapo misonkhano inanso m’Chingelezi ndi Chitumbuka. Tili okondwa kulemba mmusimu masiku ndi malo a msonkhano kumene mipingo yagaŵidwa kukapezekako. Ino ndiyo nthaŵi yoyamba kukonzekera. Amene ali pantchito yolembedwa apemphe tchuti nthaŵi idakalipo.
Masiku ndi Malo a Msonkhano Wachigawo wa 1999
August 6-8
BLANTYRE Chingelezi M-11 (Mpingo umodzi), M-23 (Mpingo umodzi)
August 13-15
BLANTYRE Chichewa M-23, M-20 (Mipingo 4), M-21 (Mipingo 13)
KANYERERE Chichewa M-7
LINTHIPE RIVER Chichewa M-14, M-15
MANGOCHI Chichewa M-18
NKHONYA Chichewa M-21, M-22
August 20-22
CHILEKA T/C Chichewa M-9, M-12
KAMPEPUZA Chichewa M-16, M-17
KANDE Chichewa M-3 (Mipingo 13), M-5 (Mipingo 4)
MWANZA Chichewa M-24
SONGANI Chichewa M-19, M-20
August 27-29
LILONGWE Chichewa M-10, M-11, M-13
LISASADZI Chichewa M-6, M-8
MZUZU Chichewa/Tumbuka M-1, M-2, M-3 (Mipingo 13) M-4
NKHOTAKOTA Chichewa M-5 (Mipingo 19)
Kumene madera agaŵidwa, mipingo yokhudzidwayo idzalemberedwa kalata yoidziŵitsa za msonkhano umene akuyenera kupita.