Ndandanda ya Mlungu wa July 6
MLUNGU WOYAMBIRA JULY 6
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 22 ndime 1-8
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Levitiko 17-20
Na. 1: Levitiko 19:1-18
Na. 2: Kodi Tonsefe Tinali Kudziko la Mizimu Tisanabadwe Ngati Anthu? (rs-CN tsa. 203 ndime 2 mpaka tsa. 204 ndime 2
Na. 3: Tisakhale Akuba (lr-CN mutu 24)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph.5: Zilengezo.
Mph.10: Zosowa za pampingo.
Mph.10: Funsani akulu kapena atumiki othandiza awiri kapena atatu. Kodi n’chiyani chinawalimbikitsa kufuna ntchito yabwino imeneyi? (1 Tim. 3:1-9) Kodi analimbikitsidwa ndi kuthandizidwa bwanji ndi anthu ena? Kodi ndi madalitso otani amene apeza?
Mph.10: Kuthandiza Ena Kuika Ufumu Patsogolo. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, pamutu waung’ono patsamba 281.