Ndandanda ya Mlungu wa August 31
MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 31
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 25 ndime 1-11
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Numeri 17-21
Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph.5: Zilengezo.
Mph.10: Mafunso Othandiza Munthu Kuganiza Ndiponso Kulankhula za Kukhosi Kwake. Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 237, ndime 3, mpaka tsamba 238, ndime 5. Mungachite chitsanzo chosonyeza mmene mungagwiritsire ntchito mfundo imodzi kapena ziwiri za m’nkhaniyi.
Mph.20: “Misonkhano Yokonzekera Utumiki Wakumunda.” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.