Ndandanda ya Mlungu wa April 5
MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 5
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Samueli 16-18
Na. 1: 1 Samueli 18:1-16
Na. 2: Kodi Tiyenera Kukumbukira Chiyani Tikamaganizira Zochitika pa Khirisimasi? (rs tsa. 241 ndime 1-3)
Na. 3: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Ochereza? (Aroma 12:13)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 12: “Zimene Aliyense Angachite Pothandiza Ntchito Yolalikira Padziko Lonse.” Nkhani yokambirana ndi omvera.
Mph. 8: Zosowa za pampingo.
Mph. 5: Bwererani kwa Anthu Achidwi Amene Anafika pa Chikumbutso. Nkhani. Tchulani chiwerengero cha anthu amene anafika pa Chikumbutso ndiponso zokumana nazo za panthawiyi. Limbikitsani onse kuti apange maulendo obwereza kwa anthu achidwi amene anafika pa Chikumbutso ndipo cholinga chawo chikhale kuyambitsa maphunziro a Baibulo. Awaitanirenso kunkhani ya onse yapadera ya panyengo ya Chikumbutso. Chitani chitsanzo cha zimenezi.