Ndandanda ya Mlungu wa September 13
MLUNGU WOYAMBIRA SEPTEMBER 13
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Mafumu 16-18
Na. 1: 2 Mafumu 17:1-11
Na. 2: Kodi Yehova wa mu “Chipangano Chakale” Ndi Yesu Khristu wa mu “Chipangano Chatsopano”? (rs-CN tsa. 421 ndime 8–tsa. 422 ndime 3)
Na. 3: Kodi Baibulo Limatiuza Kuti Tizingokhulupirira Mulungu Popanda Umboni Ulionse?
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: Mwayi Wokhala Mtumiki wa Uthenga Wabwino. Nkhani yolimbikitsa yochokera m’buku la Gulu, tsamba 77 ndi 78, ndime 2.
Mph. 15: “Lemekeza Yehova ndi Chuma chako.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho.