Ndandanda ya Mlungu wa January 10
MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 10
Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 1, ndime 1-7 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Mbiri 33-36 (Mph. 10)
Na. 1: 2 Mbiri 34:12-21 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Tingaphunzire Chiyani kwa Mariya, Mayi a Yesu? (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Yesu Anali Chabe Mtsogoleri Wachipembedzo?—rs tsa. 424 ndime 3 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 15: Muzilankhula Mwaubwenzi Polalikira. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki tsamba 118, ndime 1, mpaka tsamba 119, ndime 5.
Mph. 15: “Ntchito Yosangalatsa Kwambiri.” Mafunso ndi mayankho. Mwachidule funsani wofalitsa kuti afotokoze chimwemwe chimene wapeza pokhala ndi phunziro la Baibulo lopita patsogolo.
Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero